Mdera Langa Project

Mdera Langa Project Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Mdera Langa Project, Community Organization, Mzuzu, Johannesburg.

12/09/2026

Anthu ambiri timakumana ndi zovuta zochuluka pa moyo wathu kaamba kaumphawi, kutha kwa chikondi, kusalidwa komanso zina zambiri.

Ndipepha aliyense kuti ayambe kutsatira page ino zambiri zizikambidwa ndipo ena muzipeza chithandizo.

zikomo.

12/09/2026

Tiyamba kukambirana zamalingaliro amubongo posachedwa. please follow us.

02/09/2026

Nde akuwuze chatha ndikukapezanso kwanu sanaphike, nde umakhala wafatu kuwiri.💔

26/08/2026

Chitsime chakuya chimadziwika chikaphwa, Chakwera uja ndi dolo🙌

28/06/2026

Nde apa boma lowuma mutu ndi liti ? chakwela uja ndi second gwazi muno mmalawi. chifukwa anakwanitsa kusakweza mitengo mu thawi yomwe zithu zinali kusitha kukwera mitengo pa dziko lose lapasi. koma awa atsizina tole Dpp awononga kale dzikoli pa 9 months chosecho kulibe khondo, covid ,cyclone,.

= mu thawi ya Dr Laz 💯

- Feteleza: K120,000
- Petrol: K2.5/litre
- Mazila: K200
- Sugar: K2.5
- Soya Pieces: K500

=mkulukuta moyo.

- Feteleza: K220,000 ↑
- Petrol: K6.7/litre ↑
- Mazila: K650 ↑
- Sugar: K6.5 ↑
- Soya Pieces: K1.500

Thawi ya Chakwera 2020-2024:
Nthawi ya "Data bundle prices

- 1GB Daily: K1,500
- 1GB Weekly: K2,000
- 1.2GB Monthly: K2,500
- Malawi anakhala #1 ku Africa: 1GB = $0.38 chokha, kutsika ndi 99% kuyambira 2020

2026: Mitengo yapano pa Airtel

- 1GB Daily: K1,800
- 1GB Weekly: K2,500
- 1.2GB Monthly: K3,500
- 2GB Monthly: K5,000
- 10GB Monthly: K15,500 92bc

VOTE YANGA✅ Hon. Precious Ufulu Kabambe !ZIFUKWA ZOVOTELA PRECIOUS KABAMBE 1. CDF NDIYOCHOKELA MU BUDGET NDIPO IMAPITA K...
24/06/2026

VOTE YANGA
✅ Hon. Precious Ufulu Kabambe !

ZIFUKWA ZOVOTELA PRECIOUS KABAMBE

1. CDF NDIYOCHOKELA MU BUDGET NDIPO IMAPITA KWA MP ALIYENSE WA BOMA NGAKHALE OTSUTSA SIMUTINAMIZANSO!!!

2. NGONGOLE ZA MEDF NDI ZA ALIYENSE CHIFUKWA ZIDZACHOKA MU CDF KUDZELA MWA PRECIOUS YEMWEYO SIMUTINAMIZANSO

3. ZA FERTILIZER PALI NDONDOMEKO YOKHAZIKIKA KALE YOLEMBELA ANTHU OVUTIKA OSATI MA KUPONI A BODZA SIMUTINAMIZANSO!!!

4. KUMANGA PRECIOUS, KUMUPEKELA NKHANI SIMUTINAMIZANSO!!!

5. MWANA WA M'MUDZI MUNO AMATIDZIWA SANATITHAWEPO

6. MA BILIJI NDI MISEWU AMATIKONZELA NDI PRECIOUS KABAMBE ZAKA ZISANU ZONSEZI

7. ZAKA ZISANU WATISAMALA MU NYENGO ZOSAUTSA

8. LERO AMBULANCE USIKU NDI USANA IMAPEZEKA CHIFUKWA CHA PRECIOUS KABAMBE

WA MMUDZI
30 JUNE KUCHEMA

The President for Mighty MCP Dr Lazarus McCarthy Chakwera.
24/06/2026

The President for Mighty MCP Dr Lazarus McCarthy Chakwera.

20/06/2026
17/06/2026

Full-Time
Portugal 1-1 DR Congo
⚽️ Neves 6'
⚽️ Wissa 45+5'

17/06/2026



Nduna zonse za dziko la Equatorial Guinea zatula pansi udindo zitalephera kukwaniritsa mfundo za chitukuko zimene zinakhazikitsa.

Wachiwiri kwa mtsogoleri wa dzikolo Teodoro Obiang Nguema Mbasogo yemwe ndi mwana wa mtsogoleri, wati nduna yaikulu ya dzikolo yavomereza kuti ndunazi zalephera kukwanitsa ngakhale 10% ya mfundozo.

Zina mwa mfundozo ndi monga kutukula ntchito za ulimi komanso kuchepetsa kudalira katundu wopangidwa mmmaiko ena.

Kutsatira izi mtsogoleri wa dzikolo akuyembekezeka kusankha nduna zina zatsopano.

Wolemba Florence Mwale

Address

Mzuzu
Johannesburg

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Mdera Langa Project posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share