Friends of APM

Friends of APM Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Friends of APM, Nonprofit Organization, Johannesburg.

Akayanjana,alekeni.🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼
09/12/2025

Akayanjana,
alekeni.
🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼

BREAKING NEWS . Former SPC Collen Zamba arrested.More details to come.
06/12/2025

BREAKING NEWS .
Former SPC Collen Zamba arrested.
More details to come.

A district Governor a DPP a kasungu ndonda, a Davie Banda avulazidwa ndi achifwamba usiku wapitawu ndipo alandidwa njing...
06/12/2025

A district Governor a DPP a kasungu ndonda, a Davie Banda avulazidwa ndi achifwamba usiku wapitawu ndipo alandidwa njinga ya moto,apapa agonekedwa mchipatala pa Mtunthama ku Angrican.

Agalu Aja anagulidwa Ku South Africa . Ndi agalu oooophya Kwambiri. Anawagula for Inside Security ya President ndi Ku ma...
27/11/2025

Agalu Aja anagulidwa Ku South Africa . Ndi agalu oooophya Kwambiri. Anawagula for Inside Security ya President ndi Ku ma function a President. Amene Aja ndi a Police ndithu🚨 .

Amawatcha kuti Officers ndithu Ali ndi Maina ndi police number ndithu . Ndi thambi ndithu yina ya Police . Apopo Mlandu wake ndi Kuba Police Officers .

Apolice akusaka saka a police anzao amene asowa . That's the issue .

Iwe ukuona ngati galu koma achitetezo akuona Trained expatriate Police Officers

Ngati agaluwa anachita kugulidwa kunja you can understand how important and delicate they are .

It's very embarrassing kuti mpakana Kuba agalu .

Amabungwe chonde ndithandizeni-JessieMneneli wa Chipani cha MCP Mayi Jessie Kabwira wati akupempha a Mabungwe amuthandiz...
11/11/2025

Amabungwe chonde ndithandizeni-Jessie

Mneneli wa Chipani cha MCP Mayi Jessie Kabwira wati akupempha a Mabungwe amuthandize pa nkhani yokhuza a chinyamata a MCP omwe amangidwa pa nkhani yomenya, kukhapa anthu ndikuotcha ma Galimoto. Anthuwa adamangidwa sabata latha atagwidwa ndi a police pamene amabisala ndipo akuyimbidwa milanduyi.

Kabwira wati ndiwokhumudwa ndi mmene mulandu wa anthuwa ukuyendela kamba akawapatsa bail nthawi yomweyo police ikumawamangaso kuwawonjezera mulandu wina zomwe iye akuti akuwaphera ufulu anthuwa ndipo akupempha mabungwe amuthandizire pomumenyera nkhondo yomuthandiza kutulutsa anthu amangidwa awa.

Mmbuyomu Jessie Kabwira adati ku MCP kulibe achinyamatawa omwe akuchita za uchifwamba ndipo anthu aku a DPP komaso ochita ziwonetsero amamenyana ndikukhapana okhaokha, zomwe lero zabweretsa mafunso ochuluka Poona Kabwira akubwera kudzamvera milandu ya uchifwamba omwe amaukana uja.

Wolemba-Petro Jack.

Mai Zione Adamu aku Chamama,awona zakuda atathibulidwa ndi mkazi mnzao mpaka kutemedwa ndi phwitika,atawapedzerera akuch...
11/11/2025

Mai Zione Adamu aku Chamama,
awona zakuda atathibulidwa ndi mkazi mnzao mpaka kutemedwa ndi phwitika,
atawapedzerera akuchita kusaweruzika ndi mamuna wa mwini pa tchire lina kumeneko.
Mayiyu yemwe ndi ana atatu,koma onsewo bambo ake ake,ali kharidwe lothyolera khosi amuna a eni maka akawaona kuti ali ndi ndalama.
Patsikuli anakumana nazo mwini mamuna atayamba kuvumbulutsa zibakera mwakathithi mpaka mnzakeyo thapsa.
Chenjezo:
mnyumba ya weni sawotchera mbewa.

Zambia 🇿🇲. Zomvetsa chisoni.Mtsikana wazaka 8 yemwe ndiochokera m'boma la Nsama mdziko la Zambia 🇿🇲 wamwalira atamenyedw...
23/10/2025

Zambia 🇿🇲.

Zomvetsa chisoni.

Mtsikana wazaka 8 yemwe ndiochokera m'boma la Nsama mdziko la Zambia 🇿🇲 wamwalira atamenyedwa ndi aneba ake kamba koti amathyola mango 🥭 osapsya.

Mwanayu anamenyedwa mpaka kuphedwa kamba kothyola mangowa.

19/10/2025

Kodi azibambo mukutafuna chani?

Hon. Joseph Mwanamvekha, MP, Minister of Finance, Economic Planning and Development, is in Washington, D.C., United Stat...
17/10/2025

Hon. Joseph Mwanamvekha, MP, Minister of Finance, Economic Planning and Development, is in Washington, D.C., United States of America, attending the Spring Meetings of the World Bank and International Monetary Fund.

Starting this week, the Minister of Finance has been engaging with regional and international financial institutions and development partners to deliberate on Malawi’s immediate priorities, including food security, fertiliser supply, foreign exchange, fuel, and essential medicines.

On Wednesday, Honourable Mwanamvekha met Mr. Adriano Ubisso, Executive Director of the World Bank, followed by discussions with other regional and international financial partners, focusing on short-term policy priorities, key development projects, and funding requirements.

On Thursday, 16th October, Hon. Mwanamvekha chaired the 30th Statutory Meeting of the Constituency. He later met with the World Bank Country Management Unit and the IMF Executive Director to continue discussions on development support. The day concluded with the Minister and the Governor of the Reserve Bank of Malawi attending the World Bank Group Development Committee Ministerial Lunch and Meeting, engaging with development partners on Malawi’s economic priorities.

On Friday, 17th October, the Minister and his delegation from the Ministry of Finance, Economic Planning and Development are scheduled to participate in the IMFC Breakfast and hold a Ministerial Breakfast with the Zambian Minister of Finance. They will also meet the African Director at the IMF and the Deputy Assistant Secretary at the U.S. Treasury to discuss regional economic issues and collaboration. The day will conclude with engagements with the Rockefeller Foundation and Lazard International Advisory to explore additional development support and investment opportunities.

On Saturday, 18th October, the Malawi delegation, led by the Minister of Finance, will meet with the East and Southern African Regional Vice President of the World Bank Group to further discuss regional development priorities and sustained support for Malawi’s economic programmes.

New Ministers:Agriculture, Irrigation and Water Development Roza Fatch Mbilizi.Industrialisation, Business, Trade and To...
17/10/2025

New Ministers:
Agriculture, Irrigation and Water Development Roza Fatch Mbilizi.
Industrialisation, Business, Trade and Tourism: George Patridge

Mwina ndi abale anu koma apezeka ataphedwa ku jubeki
14/10/2025

Mwina ndi abale anu koma apezeka ataphedwa ku jubeki

Mumadzitama kuti ndinu andalama,yet kumaba fertilizer wa amalawi osauka kumathira kuminda yanu,kenako after kukolora ndi...
13/10/2025

Mumadzitama kuti ndinu andalama,yet kumaba fertilizer wa amalawi osauka kumathira kuminda yanu,kenako after kukolora ndikusunga kuti mudzagulitse mitengo yokuba,
Nthawi yanu yatha,
Its pay day.....

Address

Johannesburg

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Friends of APM posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share