Anoh Kay and Grace foundation

Anoh Kay and Grace foundation Thank you for contacting anoh Kay and Grace foundation God bless you how can help you

28/08/2024

Lets fixing our community and villages Anthu mamidzimu ndmadelamu akuvutika not bcoz of only government aiii sanje kmaso kuipa ntima kwa Anthu ena mamidzimu kukukolezela uphawi madele ndmamidzimu tatiyen tidzikondana ndkufunila zabwino ngat amalawi ndpo tidzatukuka osadikilaso boma wina akamalimbikra tiyen tithandzane naye kaya akugulitsa malonda tiyen timugule k*t moyo wake udzipta chitsogolo ngat sitingasinthe kaganizidwe uphawi udzakhala bwez lathu ngat dziko stop fighting one another lets fighting with poverty πŸ™πŸ™πŸ™ sanje kaduka dzimapha stop it may God bless our beloved malawi πŸ‡²πŸ‡ΌπŸ‡²πŸ‡ΌπŸ‡²πŸ‡Ό

Address

Durban

Telephone

+27813529953

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Anoh Kay and Grace foundation posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share