Anemed Community Based Organization. -Acobo

Anemed Community Based Organization. -Acobo Anemed Community Based Organization is a youth-led CBO in the area of Traditional Authority Mwambo in Zomba district of South Eastern MALAWI.

The organization’s background can be traced from 2016 when a group of determined young people came together with the aim of coming up with solutions to the challenges faced by the community with a biased focus on young people, women, girls and children. ACOBO’s main focus areas include Education, health and economic empowerment, targeting children, adolescent girls and young women (AGYW) and the y

outh in general. We implement activities that are aimed at improving the quality of education at early childhood and primary levels, but also improving the quality of health care services delivery for children, adolescent girls and young women AGYW and women in general... ( P.O BOX 121,JALI Zomba)

05/01/2026

TIDZIWITSE MAKOLO ONSE , KUTI SUKULU TATSEGULIRA LERO, NDIPO ANA AMENE AKWANITSA DZAKA ZOYAMBA NKOMBA PHALA, ABWERE MALO ALIPO NDITHU. TIPEZENI PA 9 MILES, KUSELI KWA CHIGAYO CHA NGALU (NZERU ZA ANGANGA MAIZE MILL)

maphunziro ndi tsogolo la mwana wathu

15/10/2025

Moms are like superheroes, they make us feel safe and happy,

HAPPY MOTHERS DAY TO YOU ALL

12/10/2025

tikuthokoza Partners In Action For Sustainable Development, potipatsa chakudya cha term ino, izi zithandiza kuti ana ku dera lathu akhale olimbikira kubwera kusukulu , komanso kukhala athanzi.

ife a ANEMED CBO,  tili achisoni pa za imfa ya yemwe anali mmodzi mwa aziphunzitsi a ku nursery yathu mu czaka zapitazi,...
06/10/2025

ife a ANEMED CBO, tili achisoni pa za imfa ya yemwe anali mmodzi mwa aziphunzitsi a ku nursery yathu mu czaka zapitazi, uthenga wa maliro watipeza lero madzulo omwe ano. ife tonse pamodzi ndi executive yathu , tili odzadzidwa ndi chisoni ndi imfayi.

mzimu wawo sister Mary Tambala uwutse muntendere.

21/09/2025

*ANEMED CBO*

pa 22 september pamene ma school azitsegulilidwa, ifenso a anemed cbo tikutsegulira NURSERY SCHOOL yathu. Bwerani ndi ana anu tidzawaphunzitse.

Ana omwe achokera pa anamed school kupita ku primary akuchitako bwino. Ana amene tawasata akhala ma number 1 up to 10.

*bwerani ndithu kantengo kolipilira mwaba wanu ndi pang'ono, mulibe timavomera kumalipila pang'ono pang'ono , mwasoweratu timatha kumupezera omulipilira*

WE ARE MOVING FORWARD

25/07/2025
Dzulo ndi tsiku lomwe sukulu yathu ya nkomba phala yatsekera maphunziro.Ndipo panali ana 93,  ambiri akukayamba primary....
25/07/2025

Dzulo ndi tsiku lomwe sukulu yathu ya nkomba phala yatsekera maphunziro.

Ndipo panali ana 93, ambiri akukayamba primary. Tithokoze makolo onse omwe munatikhulupilira kubweretsa ana.

Registration iyambika mwezi wa mmawa.

Bwerani ndi ana anu, nawonso alandire maphunziro ankomva phala

Zaka za mbuyomu, tidakhalapo ndi ma trainings , omwe tidaphunzitsa anthu mwa ulele kapangidwe ka mankhwala pogwiritsa nt...
06/07/2025

Zaka za mbuyomu, tidakhalapo ndi ma trainings , omwe tidaphunzitsa anthu mwa ulele kapangidwe ka mankhwala pogwiritsa ntchito maluwa komanso mitengo yomwe timadzala pakhomo. Maphunzirowa adachitikira pa mbidi primary school, komanso mmudzi mwa ntagaluka. Panopa tili ndi chikonzero chophunzitsa anthu kapangidwe ka SOAP monga mmene zilili pa chithunzipa. Ophunzira ndi wina aliyense ofuna kutero. Zonsezi zidzachitika mwa ulele. Tsiku lamaphunziro tidzalengeza. Chofuna kudzatenga patsikuli ndi polemba ndi cholembera

ZIKOMO

26/06/2025

Dzulo talandila mbale zodyera ana, mbalezi zitithandiza kuchepetsa vuto la mbale zomwe zimatichepera kamba ka kuchuluka kwa ana.

Tithokoze a MP athu a zomba likangala mayi ABGAIL BONGWE potipatsa thandizoli.

Amayi pitilizani ntchito zachifundo mmachitazi, tipemphenso kuti ngati nkotheka FIKIRANI ma cbo ambiri omwe ali ndi chidwi chophunzitsa ana a nkomba phala.

Ulemu wanu AMAYI

30/05/2025

Address

Jali/Phalombe Road
Zomba

Opening Hours

Monday 08:00 - 17:00
Tuesday 08:00 - 17:00
Wednesday 08:00 - 17:00
Thursday 08:00 - 17:00
Friday 08:00 - 17:00
Saturday 08:00 - 12:00

Telephone

+265999853215

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Anemed Community Based Organization. -Acobo posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Organization

Send a message to Anemed Community Based Organization. -Acobo:

Share