DON DADA INTER-10-MENT

DON DADA INTER-10-MENT Found of averything like video show,burning,disco show,beer,groceries and barber shop

25/02/2026

CHE KALONDA

Don't get too comfortable iyayi
Basi kumakhala, kumazinamiza ayi ine ndi wakuti wakuti
Ine ndi ndani ndani,...eeh aise iwe
Dziko limasankhatu kuti awa akhale mbali ya uku
Awa akhale mbali ya uku
Dziko limasankha si chirichonse mukuyenela kupanga nawo
Penapake kungovomeleza kuti alipo ena ake
Anthu osankhidwa

Kukankha mukukankha, koma simumatha
Tiziti mwayiwala, ufumu ndi wanga

VERSE 1

My reign is forever, forever ever
Makape ndawaona listiro
Ngini yake itiyo mukusibwirayo
Nyimbo zonse nthabwala ngati Winiko
Kamandinyasa ine ndi ka chisimo
Kofuna kufufuta mbiri ko
Munthu mnali p***a when they popped out
I am the one that cut the umbilical
Koma now I don't feel the connection
And these are my offspring, its spiritual
Like channeling Biggie & Pac
You'd swear these verses are off of a ouija board
Game inasolobana rappers are anything kupatula lyrical
Busy kutibwaka ngini zopanda flavor, zopanda nsinjiro
Komabe, sititopa kukankha, Mentality ya mamba
Delivery ya azamba, calmness ya kachamba
When you're this real and you've been him
Magaye sasowa chokamba
Koma 3 minutes and change on a track
popanda chimene tamva

HOOK with PRINCESS MULTIKEY

Magaye muzitolele
Hold my crown, I'm holding it down
I'm the ring master, enawa ma clown
We set the pace, they follow the sound
Tagwira, tagwira, tagwira kaye x3
Zoti ndiine shatta, usayiwale

VERSE 2

Kuti tifike pogawana nkate,
its got to be worth while
Mafana akhate kufuna kutchuka
touching my textile
Akukudandaulani ma fan, ma bundle kubetsa
Mumathadi ku flexa, koma
zanyimbo zokhazo tikhoza kuletsa
Mwati, wanyamula mbendera nda?
Akungoyimba nyimbo zobela nda?
Madolo akumvera nda?
Akuchita kumveka kugwera nda?
Mwachuluka kuvekana ma title atambwali kumetana
Ena mpaka anasiya kutifila chifukwa tinakana ku worka nawo
I understand the agenda, magaye amawona ngati zophweka
Pano, akulakalaka titasiya, mwina nawo ndikumveka
But, osandiyankhula, maka maka ndikautunga
Mphwanga tasuntha, osamakuwa
BP yanga sichedwa 🏹

Address

Changalume
Zomba

Telephone

+265884577290

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when DON DADA INTER-10-MENT posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Organization

Send a message to DON DADA INTER-10-MENT:

Shortcuts

Share