01/12/2025
Good afternoon ma friends nonse pano pa Mpiri youth Watch forum,tati tilpnjeze kuyambiranso kugwira ntchito titapumira kwa kanthawi kaamba ka zovuta zina.
Pofuna kukonzanao dongosolo lathu tithe kugwira ntchito mwapamwamba choncho kwa amene ali kufupi ndi ku mpiri tikhala ndi nkumano wosankha atsogoleri choncho konzekani nkati mwa mwezi uno wa December, mu umodzi muli mphamvu.