Feeds the World

Feeds the World Charity with a Heart | Mr Feed's Mission to Feed, Educate & Love. | Philanthropist | Humanitarian | Changing Lives | Join my mission to make a Difference .
(8)

Let's keep spreading Love around the World. Let love lead 1 Corinthians 16:14

04/05/2026

Chiwanda Chake Chosamvatu.

The type of demon very stubborn ๐Ÿ˜‚

04/05/2026

Prayer and Deliverance time.
Kumasulidwa Ziwanda.

02/05/2026

Sylvia the akutikumbutsa kuti Giving is a ministry ndipo tiyeni tikhale achikondi wina ndi mzake.

Meet Vincent. He is a homeless street Kid who sleeps near church and eat leftovers from the church guests whenever they ...
02/05/2026

Meet Vincent. He is a homeless street Kid who sleeps near church and eat leftovers from the church guests whenever they throw on the trash bin. Today we met him again together with others. We shared Food to a number of homeless people today and street kids.

CHICHEWA:

Lero tili kogawa zakudya mu street, tinakumanaso ndi Mwana yemwe dzina lake ndi Vincent amene akugona mu street pafupi ndi Church. Iyeyutu amadya zotsalira zomwe anthu aku church amataya. Ineyo ndi team yanga, tikuyesesa kuti timupezere malo okhala mwanayu komaso akayambe school. Iyeyutu Ali ndi story yomvetsa chisoni. Video coming...

30/04/2026

Hello Mr feeds please hide my id
I'm a man at a certain technical college ๐Ÿฅฑkm the past two months I had unprotected s*x with the girl km paka pano after urination ndimatuluka magazi or after s*x mu condom ndumapezamo magazi please post for me I need help.

Ma dotolo ndi ma Nurse muthandizeni Mnyatayu. Nde ndi chi handsome koma kusamva .

29/04/2026

Mwamukumbukila mwanayu?
Panopa ndi momwe zilili. Kusintha kulipo.
Let Love lead. Let God be God!!
Zonse mzotheka ndi ambuye.

Mulungu wathu ndi wa moyo sangatisiye Tokha.

Ndithokoze annon pa Thandizo la Monica lija Tikusuntha. Tatsala ndi 10 mita kuti tifikile pa Mlingo wa 27.6 mita. Lero N...
29/04/2026

Ndithokoze annon pa Thandizo la Monica lija Tikusuntha. Tatsala ndi 10 mita kuti tifikile pa Mlingo wa 27.6 mita. Lero Ndathandizidwa ndi 4.7 mita kudzera Western Union.
Mawa akupanga Biopsy onse Monica ndi Mervis, akatero awapangaso Sedation kuwapanga grind kuti atenge ka fupa for ma further tests.
Ma results onse akabwela after two weeks,
Monica akuyenera kupangidwa Surgery.
Mervis Nayeso Apangidwa Surgery..
Tidikila ma results a biopsy ndi sedation abwere Kaye koma.

Ndalandira K5.6 mita kuchokera Kwa Anonymous Iwowa Ali mu Lilongwe momwemotu. Akuti ndionjezere pa 19 mita yatsala ija. ...
28/04/2026

Ndalandira K5.6 mita kuchokera Kwa Anonymous Iwowa Ali mu Lilongwe momwemotu. Akuti ndionjezere pa 19 mita yatsala ija. Ndekuti pamenepo tatsala ndi K14 mita. Pang'ono ndi pang'ono tikwanitsa. Pangatalike bwanji koma ifika basi.

Bambo a Mervis akuti Moni Nonse.

Zikomo Annon Ku USA Florida mondithandiza ndi K5 mita kwacha. Pa 27 mita ya Monica ija, Yatsala 19 mita. Ndekuti ndatole...
28/04/2026

Zikomo Annon Ku USA Florida mondithandiza ndi K5 mita kwacha. Pa 27 mita ya Monica ija, Yatsala 19 mita. Ndekuti ndatolera K9.4 mita.

Komaso Nditaganiza, ndangoiyamba school ya ana onse omwe Ali mu ward kuti ndizithandizana nawo ma Lessons. Zojambula ndi zoletsedwa koma ndangoti mungodziwa kuti kunoko tayambaso School. Ana onsewa Ali ndi Khansa ndipo akuyenera kuoneseledwa Chikondi.

Morning Feeds family, Ndalama ija yakwana zikomo family. Ena apeleka through western union. Ndithokozeso annon popeleka ...
28/04/2026

Morning Feeds family, Ndalama ija yakwana zikomo family. Ena apeleka through western union.
Ndithokozeso annon popeleka 4.2 mita kuti tichosele pa 27 mita ya Operation ya Monica ija.
Ndikhululupilira pompano ikwana ndipo tikhala ndi testimony akamupanga operation mwana onsewa. Ineyo chikhulupiliro ndili nacho tibwelera bwino bwino tonse keep praying.

Rest in peace Davie. You fought a good fight. Till we meet again. ๐Ÿ•Š๏ธ๐Ÿ’”Kwathu sipadziko. Mzimu wako uuse mumtendere.
27/04/2026

Rest in peace Davie. You fought a good fight. Till we meet again. ๐Ÿ•Š๏ธ๐Ÿ’”
Kwathu sipadziko. Mzimu wako uuse mumtendere.

Address

Salima

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Feeds the World posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share