Wibra foundation

Wibra foundation Wibra foundation is n organization with an aim to help the needy

Kwa omwe akufuna kutithandiza atha kugwilitsa ntchito mpamba short code iyi
06/02/2022

Kwa omwe akufuna kutithandiza atha kugwilitsa ntchito mpamba short code iyi

Wibra foundation ikusaka anthu akufuna kwabwino kuti akhale abwenzi a wibra(partners) pa ntchito yomwe ikuchitika komans...
06/02/2022

Wibra foundation ikusaka anthu akufuna kwabwino kuti akhale abwenzi a wibra(partners) pa ntchito yomwe ikuchitika komanso kufuna ma volunteers(odzipereka) kwa omwe Ali ofuna chonde imani pa nambala izi 0884137180 0884176055/0884716426

Kwa abwenzi omwe angathe kumathandiza ndindalama yokwanira 500 kwacha pamwezi muli oloredwa kutiyendera nkuzaona zonse zinachitika tili pa zalewa pa ccap church kuseri kwake

01/02/2022

Empowered women are the agents of change.we are working with women groups to bring about change

Ndi 500 kwacha m***a kugulirako mwana osowa ndi wamasiye makope ndi zolembera
16/12/2021

Ndi 500 kwacha m***a kugulirako mwana osowa ndi wamasiye makope ndi zolembera

08/12/2021
As you plan to celebrate Xmas n New year consider other needy peopleWibra invites you to donate something in support of ...
14/11/2021

As you plan to celebrate Xmas n New year consider other needy people
Wibra invites you to donate something in support of vulnerable children with clothes or food items
Contact us on 0884137180/0884176055

M***a kukhala mbali imodzi yothandiza popereka 500 kwacha pa mwezi mufikira ndikuthandiza mwana winawake penapake ngakha...
08/10/2021

M***a kukhala mbali imodzi yothandiza popereka 500 kwacha pa mwezi mufikira ndikuthandiza mwana winawake penapake ngakhale mzimayi wamasiye komanso okalamba tumizani thandizolo kudzera Ku mpamba code iyi: 602025

No gift is too small give a gift of life time , transform a child s future today and you can make a difference of their ...
08/10/2021

No gift is too small give a gift of life time , transform a child s future today and you can make a difference of their life tomorrow

Be our partner in helping these children ...with 500 kwacha only
Wibra foundation mpamba short code is 602025

Wibra youth at sweeping exercise
06/10/2021

Wibra youth at sweeping exercise

Kwa omwe Ali ndi thandizo kapena akufuna kukhala abwenzi a wibra foundation pofikira anzathu ochepekedwa amasiye ndi ovu...
28/09/2021

Kwa omwe Ali ndi thandizo kapena akufuna kukhala abwenzi a wibra foundation pofikira anzathu ochepekedwa amasiye ndi ovutikitsisa kuyambira 500 Mk kupita mmwamba nayi code yathu ya mpamba....ambuye akudalitseni pamene mwatengapo gawo lothandiza ndi 500 kwacha mwezi ulionse

There's a wonderful mythical law of nature that the three things we crave most in life  -happiness,frredom and peace of ...
28/09/2021

There's a wonderful mythical law of nature that the three things we crave most in life -happiness,frredom and peace of mind are always attained by giving them to someone else,please remember the orphaned in your life activities.God will grant you more than your expectations

25/09/2021

Wibra youth club kuphunzitsana kapangidwe ka fertilizer wachilengedwe

Address

Box 33, Zalewa
Neno

Telephone

+265884137180

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Wibra foundation posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share