28/07/2026
43% of girls in Malawi are married before the age of 18.(MDHS 2024)
That's not just a statistic, it's thousands of girls whose education, health, and future opportunities are at risk.
Every girl deserves the chance to grow, learn, dream, and choose her own future. Ending child marriage requires collective action through education, community engagement, stronger protection systems, and the empowerment of girls.
Together, we can create a Malawi where every girl has the opportunity to reach her full potential.
💬 What actions do you think communities can take to help end child marriage? Share your thoughts in the comments.
Chichewa Caption 🇲🇼
43% ya atsikana ku Malawi amakwatiwa asanakwanitse zaka 18.(MDHS 2024)
Ichi si chiwerengero chokha, ndi moyo wa atsikana ambiri omwe amatha kutaya mwayi wophunzira, kukhala ndi thanzi labwino, komanso kukwaniritsa maloto awo.
Mtsikana aliyense ali ndi ufulu wokula, kuphunzira, kulota, ndi kusankha tsogolo lake. Kuthetsa ukwati wa ana kumafuna mgwirizano wa aliyense kudzera mu maphunziro, kuteteza ana, kulimbikitsa anthu m'madera, komanso kupatsa atsikana mphamvu.
Pamodzi tingamange Malawi komwe mtsikana aliyense ali ndi mwayi wokwaniritsa maloto ake.
💬 Kodi mukuganiza kuti anthu m'madera angachite chani pothandiza kuthetsa ukwati wa ana? Gawani maganizo anu mu ndemanga.
Gender JusticeMenEngage AllianceAlliance for Youth SRHR Organisations in MalawiMzuzu City Youth NetworkMishey GondweSalome KadaziMtisunge AIDS and Community Development Support Organization -MacodesoElangeni Youth OrganizationGlobal Citizen