Christ Life Education & Response

Christ Life Education & Response If you seek Wisdom and Understanding, you shall surely have them liberaly. Thus God's gift🎂

31/05/2026

Matthew 24:24 -
ⓙchifukwa Akhristu onama adzauka, ndi aneneri onama nadzaonetsa zizindikiro zazikulu ndi zozizwa: kotero kuti akanyenge, ngati nkotheka, osankhidwa omwe. Onani ndakuuziranitu pasadafike.

| For false christs and false prophets will rise and show great signs and wonders to deceive, if possible, even the elect.

31/05/2026

"May the God of hope fill you with all joy and peace as you trust in him, so that you may overflow with hope by the power of the Holy Spirit."

- Romans 15:13

26/05/2026

John 20:29 -
ⓗYesu ananena kwa iye, Chifukwa wandiona Ine, wakhulupirira; odala iwo akukhulupirira, angakhale sanaona.

| Jesus said to him, “Thomas, because you have seen Me, you have believed. Blessed are those who have not seen and yet have believed.”

26/05/2026

Mark 14:62 -
ⓨNdipo Yesu anati, Ndine amene; ndipo mudzaona Mwana wa Munthu alikukhala kudzanja lamanja la mphamvu, ndi kudza ndi mitambo ya kumwamba.

| Jesus said, “I am. And you will see the Son of Man sitting at the right hand of the Power, and coming with the clouds of heaven.”

26/05/2026

Deuteronomy 4:6 -
ⓕChifukwa chake asungeni, achiteni; pakuti ichi ndi nzeru zanu ndi chidziwitso chanu pamaso pa mitundu ya anthu akumva malemba ndi kuti, Ndithu mtundu waukulu uwu, ndiwo athu anzeru ndi akuzindikira.

| Therefore be careful to observe them; for this is your wisdom and your understanding in the sight of the peoples who will hear all these statutes, and say, ‘Surely this great nation is a wise and understanding people.’

23/05/2026

Micah 7:18 -
ⓘNdani Mulungu wofanana ndi Inu, wakukhululukira mphulupulu, wakupitirira zolakwa za otsala a cholowa chake? Sasunga mkwiyo wake kunthawi yonse popeza akondwera nacho chifundo.

| Who is a God like You, Pardoning iniquity And passing over the transgression of the remnant of His heritage? He does not retain His anger forever, Because He delights in mercy.

21/05/2026
21/05/2026

Matthew 18:22 -
ⓒYesu ananena kwa iye, Sindinena kwa iwe kufikira kasanu ndi kawiri, koma kufikira makumi asanu ndi awiri kubwerezedwa kasanu ndi kawiri.

| Jesus said to him, “I do not say to you, up to seven times, but up to seventy times seven.

21/05/2026

Matthew 18:21

Pamenepo Petro anadza, nati kwa Iye, Ambuye, mbale wanga adzandilakwira kangati, ndipo ine ndidzamkhululukira iye? Kufikira kasanu ndi kawiri kodi?

Then Peter came to Him and said, “Lord, how often shall my brother sin against me, and I forgive him? Up to seven times?”

Address

Mzuzu
SOLIER

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Christ Life Education & Response posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share