10/09/2026
Tinatenga nawo mbali pa mwambo wotsegulira Chinsapo Health Centre Extension, womwe unatsogozedwa ndi AHF Malawi, mogwirizana ndi Ministry Of Health - Malawi Ministry of Local Government and Rural Development komanso Lilongwe City Assembly.
Ntchito yathu inali kuthandiza pa documentation ya mwambowu, makamaka kujambula zinthuzi komanso kusonkhanitsa video highlights
Mwambowu ndi chitsanzo cha mgwirizano pakati pa boma ndi mabungwe achinyamata popititsa patsogolo nkhani zaumoyo m’dziko muno kudzera mu digital.
Onerani ma highlights omwe tinajambula a mwambowu pa link ili m'munsimu.
https://youtu.be/654CjgH2KT0?si=ZsPSE_YLmcP_8yb-
Note: Content yi ndi ya AHF Malawi ndi Malawi Government .
Kwathu ndikujambula chabe.