02/09/2025
SEPTEMBER IS SU***DE PREVENTION MONTH💚
Zomvetsa chisoni kuti tikupitiliza kutaya young souls to su***de maka-maka pa nkhani ya heartbreaks from relationships:
Achinyamata, dziwani izi: Kuti mfike pamsinkhu pomwe mulipo, Komanso kutha kupanga zinthu zosiyanasiyana zomwe inu mumakonda, being at school or work or various social settings, zinatengera kukondedwa kwambiri ndimakolo athu, right from our mother's wombs mpaka lero...
Tisaphe chikondi chopambana kuchokera kwa Mulungu, makolo kapena kholo, achibale ndi anzathu that helped us reach this far pa moyo wathu, just because of a boyfriend-girlfriend relationship yomwe tangokhalamo for 2 or 3 years...Tisaononge Zaka '25' za chikondi chopambana because of a heartbreak kuchokera kwa munthu yemwe watipeza titakula kale, woti tangodziwana naye for 2 or 4 years.
We are so BIG, We are so Loved, so Valuable and so Lovely, that's why winayo anagwa nafe mchikondi.
There is always gold from God waiting for you.
Yes, the heart breaks when relationships go wrong...But Time Heals, Uluru umatha ndi nthawi...Dzikoli likanatha kalekale ngati makolo athunso anali ndi Mtima wonyanyala moyo after every single heartbreak...Bwenzi Dzikoli ndi Manda ndi mitembo yokha-yokha.
Talk to us, talk to someone with a mature and caring heart & mind, someone with a listening ear and a supportive heart...But su***de shouldn't be an option...Time is a Healer. Your sun will always rise - shine again 💚🤗