UTM Affiliates Central Region Chapter

UTM Affiliates Central Region Chapter Central Region UTM Affiliate s Chapter

*Dr Dalitso Kabambe*☆World Press Freedom Day☆ UTM imayima ndi atolankhani. Chifukwa popanda ufulu wa atolankhani, palibe...
03/05/2026

*Dr Dalitso Kabambe*

☆World Press Freedom Day☆
UTM imayima ndi atolankhani. Chifukwa popanda ufulu wa atolankhani, palibe demokalase.

*TSOGOLO LATHU* 🇲🇼

☆ *SUKULU IMAYENDA BWINO NDI MKHUTO* ☆Ana a sukulu, makamaka aku Secondary, akusowa zambiri.*Amayi Ticheze UTM Affiliate...
02/05/2026

☆ *SUKULU IMAYENDA BWINO NDI MKHUTO* ☆

Ana a sukulu, makamaka aku Secondary, akusowa zambiri.
*Amayi Ticheze UTM Affiliate* ayankhapo ndikuchitapo kanthu pothandiza pa mavuto ena.

Pa chithunzichi, akugula zakudya za mitundu yosiyanasiyana — chifukwa *mtsikana wathanzi ndi yemwe angakwanitse kuphunzira bwino.*

*Iyi ndi ntchito ya UTM Media Affiliates:*
Kuwonetsa dziko ntchito zachifundo zomwe ma group athu akugwira. Kuchokera ku yunifolomu, makope, mpaka chakudya.

Tikugwira ntchito limodzi ndi ma media team a UTM onse monga *Painkiller, UTM Media, DK Forces* — kuti nkhani yabwino ifikire aliyense pa Malawi pano and beyond.

*Dr Dalitso Kabambe* anati maphunziro ndiwo tsogolo. Amayi Ticheze akukwaniritsa.

📚 *MAPHUNZIRO NDIE TSOGOLO* 📚 Amayi Ticheze, UTM Affiliate aku gwila ntchito yotamandika apa tikuona leader ship ya amay...
02/05/2026

📚 *MAPHUNZIRO NDIE TSOGOLO* 📚

Amayi Ticheze,
UTM Affiliate aku gwila ntchito yotamandika apa tikuona leader ship ya amayi ticheze. iku gwila ntchito yo gawa zipangizo kwa ana a Primary ndi Secondary , apa akulandira yunifolomu, makope,komaso zolembera ,zida zomenyera tsogolo lawo.

☆Amayi Ticheze akugwira ntchito ngati nyerere☆ mwakhama, mwadongosolo, osatopa. Cholinga ndi chimodzi: kufikira boma lililonse mdziko muno.

☆Chifukwa chiyani?☆
1. Kuchepetsa mavuto omwe ana akukumana nawo pa sukulu
2. Kukwaniritsa manifesto ya chipani cha UTM
3. Kukwaniritsa masomphenya a Malawi pa nyengo ino ya ziyangoyango

Motsogozedwa ndi ☆Dr Dalitso Kabambe☆ President wa UTM, gulu ili lati: _“Sitikubwelera mmbuyo. Khumbo lathu ndikuti mavutowa athetsedwe mtsogolomu.”_

Tiyeni tithandizane kumanga Malawi 💪🏾

☆Amayi Ticheze manja mwanu ☆🔥🔥🔥.Meet :☆Clara Janet Kamwatso☆wamaliza Degree ku MUBAS! Zonsezi chifukwa cha *Gulu La Amay...
01/05/2026

☆Amayi Ticheze manja mwanu ☆🔥🔥🔥.

Meet :
☆Clara Janet Kamwatso☆wamaliza Degree ku MUBAS!

Zonsezi chifukwa cha *Gulu La Amayi Ticheze*
UTM Affiliates. Anamulipira sukulu yonse mpaka ku mvula gown lero.

Clara akuti,
Zikomo Amayi Ticheze ndi atsogoleri athu. Pitirizani ntchito yabwinoyi.
Tsiku lina adzathandizenso ena.

*Amayi Ticheze* akupitiriza kuthandiza atsikana amene akusiya sukulu chifukwa cha umphawi. Cholinga? Kuthetsa maukwati a ana ndi kukwaniritsa masomphenya a UTM motsogozedwa ndi
*Dr Dalitso Kabambe*

Ngati njira imodzi yokwaniritsa zomwe analonjeza  nthawi ya misonkhano yokopa anthu wachiwiri kwa Mtsogoleri wachipani C...
10/03/2026

Ngati njira imodzi yokwaniritsa zomwe analonjeza nthawi ya misonkhano yokopa anthu wachiwiri kwa Mtsogoleri wachipani Cha UTM Dr Alexander Masankho Bulirani posachedwapa wapereka MJigo ku dera la Nachitheme Boma la Ntcheu.
Pakali pano olemekedzeka a Bulirani akumanganso office yomwe izigwira ntchito ngati malo ogwirira ntchito a police pa Salima Turn off.🔥🔥🔥🔥 UTM maso pa sogolo ndi DK.

Mary Chilima, wife of the late Dr. Saulos Chilima, has welcomed the announcement of a fresh inquiry into the plane crash...
24/02/2026

Mary Chilima, wife of the late Dr. Saulos Chilima, has welcomed the announcement of a fresh inquiry into the plane crash that claimed her husband’s life, while expressing gratitude to former President Prof. Arthur Peter Mutharika for his support.

The statement follows remarks by the Minister of Justice, Charles Mhango who confirmed that a new investigation into the tragic crash will be conducted to ensure accountability and transparency.

In her message, Mrs. Chilima said, “Zikomo kwambiri, kwabasi, Your Excellency Prof. Arthur Peter Mutharika. God bless you both, always.”

She described the move as a positive step toward uncovering the full circumstances surrounding the accident and achieving justice.

10/09/2025

Shadow Mp Ivy Zimba Dzenza constituency and Shadow councillor wa Brian Safanana Ngoma shadow councilor KABWABWA WARD

utm ndi Dr Dalitso kabambe.

shadow wachikondi ndi anthu ake ndi yemweyu Vote Dr Dalitso kabambe and Ivy Zimba.
10/09/2025

shadow wachikondi ndi anthu ake ndi yemweyu

Vote Dr Dalitso kabambe and Ivy Zimba.

UTM
10/09/2025

UTM

10/09/2025

with utm and Dr Dalitso kabambe I can a sure you malawi will never be the same.

UTM President Dr. Dalitso Kabambe confirms collapse of alliance talks. With MEC having printed ballot papers, UTM deems ...
18/08/2025

UTM President Dr. Dalitso Kabambe confirms collapse of alliance talks. With MEC having printed ballot papers, UTM deems further negotiations pointless. The party will contest the presidential election independently. UTM's decision is clear: going solo.

Address

Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when UTM Affiliates Central Region Chapter posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share