18/08/2026
Hallo good people...
Kwa omwe muli achi albino komanso muli ndi abale omwe Ali achi albino,ndipo pa thupi panu Pali mabala omwe sakupola komanso ofunika kuchotsa,kuli clinic yomwe titachite Ku Benga , Nkhotakota kuyambira pa 15-21 September 2026.
Kwa omwe muli Ku lilongwe komanso ma district ozungulira ndiimbireni phone pa 0991540406 komanso 0994883343.
Kuti mumve zambiri,zikomo