01/01/2024
Pamene tikhala mdziko, mmudzi komaso mma plot athu tidziwe kuti ndife thandizo kwa oyandikana naye uja. Kotero, tiyeni tiyesetse kukhala bwino ndi anthu onse otizungulira chifukwa zamawa szidziwika.
Usiku wabwino
Follow and like this page!