Education Zone

Education Zone Deliver academic information to those who deserve

31/07/2026

Koma kumeneko
πŸ˜‚πŸ˜‚

The JCE and PSLCE examinations have been marked, and the results will be released soon. Follow Maneb Results   so you ca...
31/07/2026

The JCE and PSLCE examinations have been marked, and the results will be released soon. Follow Maneb Results so you can easily access the results link as soon as it is available.

An IPTE 19 teacher, Alfred Chilambila, has been named Teacher of the Year at Dreamberry Private Academy in Bangwe, Blant...
24/07/2026

An IPTE 19 teacher, Alfred Chilambila, has been named Teacher of the Year at Dreamberry Private Academy in Bangwe, Blantyre.

CZ TTC SHINE WITH EXCELLENCE πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯

Popcorn business ndi imodzi mwa mabizinesi osavuta kuyamba chifukwa imafuna ndalama zochepa ndipo anthu ambiri amakonda ...
20/07/2026

Popcorn business ndi imodzi mwa mabizinesi osavuta kuyamba chifukwa imafuna ndalama zochepa ndipo anthu ambiri amakonda popcorn.

Zomwe mungafunike

Chimanga cha popcorn

Mafuta ophikira

Shuga kapena mchere (kutengera mtundu wa popcorn)

Popcorn machine kapena poto wokhala ndi chivindikiro

Ma packet kapena ma plastic bag

Sticker yokhala ndi dzina la business (ngati mukufuna kupanga brand)

Malo ogulitsa

M'masukulu

M'misika

M'ma bus station

Pa ma event (maukwati, masewera, misonkhano)

M'mashopu kapena ma supermarket ang'onoang'ono

Momwe mungapangire phindu

Mwachitsanzo:

Mtengo wopanga packet imodzi: MK500

Mtengo wogulitsa: MK1,000

Phindu pa packet: MK500

Mukagulitsa ma packet 50 patsiku, phindu lingakhale pafupifupi:

MK25,000 patsiku

Malangizo opambana

Pangani popcorn yokoma komanso yofanana nthawi zonse.

Gwiritsani ntchito ma packet aukhondo komanso okongola.

Khalani ndi mitundu yosiyanasiyana, monga sweet, salty, kapena butter flavor.

NKHANI izitha
20/07/2026

NKHANI izitha

19/07/2026

Away from education....
Inu mwakwera it?
πŸ˜‚

19/07/2026

(From inbox)

I'm in Zomba ndili ndi ma book awa english gramma bk geo complete book 3 target geo book 4 history achievers maths arise book 4 excel maths book 3 bio 3 and 4 excel agri excel 4 agri book 3 arise and ma pathlet 6 0999579539 mtengo pang'ono

NKHANI YA BWINO KWA ANTHU ONSE OKHALA KU ZOMBA NDI MADERA ENA OZUNGULIRA...Kuli holiday Classes yomwe ikuyamba pa 27 Jul...
19/07/2026

NKHANI YA BWINO KWA ANTHU ONSE OKHALA KU ZOMBA NDI MADERA ENA OZUNGULIRA...

Kuli holiday Classes yomwe ikuyamba pa 27 July mpaka pa 4 September 2026...Kupangira kuti mitu isazizire.

More information πŸ‘‡

Ngati mukufuna quality service ayeseni a     ndipo Simuzakhumudwa....FAST, ACCURATE AND RELIABLE πŸ”₯πŸ”₯More information πŸ‘‡
19/07/2026

Ngati mukufuna quality service ayeseni a ndipo Simuzakhumudwa....

FAST, ACCURATE AND RELIABLE πŸ”₯πŸ”₯

More information πŸ‘‡

Nanga angalime?? Number yawo ili pompo katundu madzi uyu ..
19/07/2026

Nanga angalime?? Number yawo ili pompo katundu madzi uyu ..

Address

Lilongwe

Telephone

+265884760228

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Education Zone posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Organization

Send a message to Education Zone:

Shortcuts

Share