Lumbadzi Youth Talents association - LYTA

Lumbadzi Youth Talents association - LYTA A step of patriotic youths towards light

Kanayo O Kanayo wa ku Malawi, Munthu Wamkulu Genuine Kado Mpeni wanga sudya Nkhwani🙌🏻
18/06/2025

Kanayo O Kanayo wa ku Malawi,

Munthu Wamkulu Genuine Kado Mpeni wanga sudya Nkhwani🙌🏻

Iran yang'amba ndikugwetsa drone ya nkhondo ya Israel yotchedwa Hermes 900 Long-Endurance Tactical UAV ku Isfahan Provin...
18/06/2025

Iran yang'amba ndikugwetsa drone ya nkhondo ya Israel yotchedwa Hermes 900 Long-Endurance Tactical UAV ku Isfahan Province usiku wathawu. Nayonso Israel Defence Force yatsimikiza kuti zachitikadi.

Koma akuchitana kanthu 🙌

Kunali anemwe❤ kalekalero💥
18/06/2025

Kunali anemwe❤ kalekalero💥

Uyu wafanana nd ndan😂
18/06/2025

Uyu wafanana nd ndan😂

  Dziko la Iran lati liri ndichikhulupiliro kuti maiko akufupi ndi iwo omwe ndi achisilamu salora kuti dziko la America ...
18/06/2025

Dziko la Iran lati liri ndichikhulupiliro kuti maiko akufupi ndi iwo omwe ndi achisilamu salora kuti dziko la America liwapange chiwembu.

Izi ndi malingana ndi Esmaeil Baghaei, mneneri woyang'anila unduna wa ubale pakati pa Iran ndi maiko ena ndipo amayankhula ndi Al-Jazeera.

Baghaei wati iwo apitiliza kuteteza dziko lawo komanso kubwenza chipongwe ku Israel ndipo ali ndichikhulupiliro kuti maiko akufupi ndi iwo salora kuti America iwapange chipongwe.

Pakadali pano anthu opitilira 35 amwalira pamene nkhondoyi yomwe akulimbana ndi nuclear yaku Iran ikupitilira.

Kwa omwe takulira ku mudzi idzizi timazitchula kuti chani?😁 🤗
18/06/2025

Kwa omwe takulira ku mudzi idzizi timazitchula kuti chani?😁

🤗

18/06/2025

Glucometer for sale.

Kwa amene mumadwala matenda a sugar kapena amene muli ndi ma private clinics pali glucometer (Machine oyezera kachulukidwe ka glucose/sugar mthupi mwanu).

Price : MK25,000 only
Call:0994797279

18/06/2025

Bola ana apano kuli ma bathing towel ife ankangotiponya m'mwamba katatu tauma😂

Good morning 🌄

The Scorchers have safely arrived in Casablanca ahead of Thursday's International Friendly match against Morocco.
17/06/2025

The Scorchers have safely arrived in Casablanca ahead of Thursday's International Friendly match against Morocco.

Atupele Muluzi, the leader of the United Democratic Front (UDF), has recently made headlines with his audacious call for...
17/06/2025

Atupele Muluzi, the leader of the United Democratic Front (UDF), has recently made headlines with his audacious call for former President Peter Mutharika to retire from the presidential race due to his age.

APOLISI AMANGA RASTA AMENE AKUMUGANIZIRA KUTI ANAWOTCHA TCHALITCHI CHA MA RAS KU MZUZU Apolisi ku Mzuzu amanga Ras Kepso...
14/06/2025

APOLISI AMANGA RASTA AMENE AKUMUGANIZIRA KUTI ANAWOTCHA TCHALITCHI CHA MA RAS KU MZUZU

Apolisi ku Mzuzu amanga Ras Kepson Wali wazaka 29 pomuganizira kuti anawotcha tchalitchi chama Ras komanso nyumba ku Mchengautuba mu mzinda wa Mzuzu usiku wapa 6 ndi 7 June,2025.

Wachiwiri kwa m'neneri wa polisi ya Mzuzu Sub-Inspector Cecelia Mfune wati Ras Wali anayambitsa maphokoso pamene amafuna udindo waukulu pa tchalitchi chama Ras chomwe chinamangidwa ku Mchengautuba ndipo anthu anamukana.

Kotero usiku wapa 6 ndi pa 7 June a Wali anapita ku tchalitchili kukachiyasa komanso kuphwanya ma window ndi khoma la nyumba yapafupi zomwe ndizandalama zokwana K4,500,000

A Mfune ati apolisi aku Mchengautuba atalandira lipoti anayamba kafukufuku ndipo awapeza a Wali lero pa 13 June, 2025 ku dera la Nambo komwe amabisala komwenso apeza jumbo yomwe munali chamba.

Pakadali pano oganizilidwayu akuyembekezereka kukaonekera ku bwalo la milandu kukayankha mulandu waupandu komanso kupezeka ndi chamba.

Address

Lumbadzi
Lilongwe

Telephone

+265887201846

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Lumbadzi Youth Talents association - LYTA posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share