Mauthenga Achisoni

Call Directions Contact the organization

Mauthenga Achisoni MAUTHENGA ACHISONI OFFICIAL FACEBOOK PAGE.

Nkhani ya chisoni😭 Apolisi ku Zomba akufufuza za imfa yomwe akuganiza kuti ndi yodzipha, pambuyo poti mtembo wa mnyamata...
30/07/2026

Nkhani ya chisoni😭

Apolisi ku Zomba akufufuza za imfa yomwe akuganiza kuti ndi yodzipha, pambuyo poti mtembo wa mnyamata wa zaka 21 wapezeka utapachikidwa pa mtengo m'nkhalango ya Malosa pafupi ndi mtsinje wa Likwenu.

Malemuwa adziwika kuti ndi a Precious James, omwe anasowa pa 16 Epulo chaka chino ndipo thupili lapezeka dzulo, zomwe zathetsa miyezi ingapo ya kusadziwika komwe anali.

Malinga ndi Mneneri wa Polisi ya Zomba, constable Andrew Mwale, wati apolisi a dipatimenti ya Criminal Investigation (CID) ochokera ku Domasi Police Post anapita kumaloko atalandira lipoti la nkhaniyi.

APolisiwa ati mtembowo unapezeka utawonongeka kwambiri, utapachikidwa pa mtengo pogwiritsa ntchito chidutswa cha nsalu chomwe akukhulupirira kuti chinang'ambidwa kuchokera pa thalauza la malemuyo.

Ndipo atalipima thupilo pa chipatala cha St. Luke's zasonyeza kuti imfayo idachitika chifukwa chosowa mpweya kaamba kopindika pakhosi.

Polisi yatinso achibale a malemuyo anatsimikizira kuti mtembowo unali wa Precious James, ndipo chilolezo chokachita mwambo wamaliro chinaperekedwa.

Precious James amachokera m'mudzi wa Mtambo, Mfumu Yaikulu Malemia m'boma la Zomba ndipo ayikidwa m'manda lero m'mudzi wa Sakata, mfumu Yaikulu Malemia m'boma lomwelo.

Source jojofm

Dax I need PSP too plz😭💔💯
24/11/2023

Dax I need PSP too plz😭💔💯

I just pray for brighter days…

Address

Lilongwe

Telephone

+265990782759

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Mauthenga Achisoni posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Organization

Send a message to Mauthenga Achisoni:

Shortcuts

Share