17/06/2023
Atsikana Kodi mwalembela kale izi.
Form ilipo yaulere pa WhatsApp 0998660370.
Mimwayi iyi ingapitilire kukupezani ku foni kwanu ngati mutakhala membala was AYODA polembetsa mwaulere motere.
1. Pangani like AYODA page.
2. Ponyani ma contacts details Anu ku inbox ya AYODA page mukatero Inu mwalembetsa.
Chonde musaike ma nambala Anu poyera monga pa comment koma ku inbox.
Tsiku lotseka kulandila ma application aumembala ku AYODA ndi pa 27 June 2023.