Ndaula Interfaith Development Club

Ndaula Interfaith Development Club Social & humanitarian

13/07/2024

Chilungamo chimamasula
Wanyenyeka uyu?

06/07/2024

A polisi m'boma la Mangochi amanga Chataika Makawa wa zaka 45 kamba komuganizira mlandu okupha mkazi wake Esimy Daudi wa zaka 42.

Amina Tepani Daudi, Mneneri wa polisi ya Mangochi wauza MIJ Online kuti Makawa anachita izi atakaikila kuti mkazi wakeyu amachita mchitidwe oyendayenda ndi amuna ena.

Malingana ndi Tepani, izi zinachitikila pa mudzi wa Kwitunji, m'dera la mfumu yayikulu Katuli m'bomalo.

Pakadali pano, Makawa yemwe ndi wa m'mudzi mwa Muyaya kwa Mposa m'boma la Machinga akuyembekezeka kuyankha mlandu okupha munthu zomwe ndi zosemphana ndi gawo 209 la malamulo owona za upandu.
-Aubrey Kalumpha-

Winter settings
24/06/2024

Winter settings

Of late these two have always been seen together, are we reading between the lines? There is a story behind the camera.
13/04/2024

Of late these two have always been seen together, are we reading between the lines? There is a story behind the camera.

20/01/2024

You notice someone online & you greet him. You receive no response yet they sought your friendship.

Or shall we say : A POOR MAN'S GREETING IS ALWAYS REGARDED AS BEGGING?

Address

Msundwe
Lilongwe

Telephone

+265997315552

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Ndaula Interfaith Development Club posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share