Malawi online

Malawi online Our aim is to inform people on what is happening in their country

Is equal to 1 bag of fertilizer malinga ndi kuyankhura kwa mtsogoleri wa dziko lino Dr Lazarus Chakwera.
20/12/2024

Is equal to 1 bag of fertilizer malinga ndi kuyankhura kwa mtsogoleri wa dziko lino Dr Lazarus Chakwera.

Msungwana uyu akulumbira cheke cheke thwaaaaa!!! Kuti Bushiri he's my biological father "I can touch the bible 📖
20/12/2024

Msungwana uyu akulumbira cheke cheke thwaaaaa!!! Kuti Bushiri he's my biological father "I can touch the bible 📖

Mtsogoleri wa dziko lino Dr Lazarus Chakwera walamula committee yomwe imafufuza ngozi ya ndege yomwe idapha wachiwiri kw...
19/12/2024

Mtsogoleri wa dziko lino Dr Lazarus Chakwera walamula committee yomwe imafufuza ngozi ya ndege yomwe idapha wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino Dr Saulos Claus Chilima ndi anthu ena kuti apereke zotsatira za kafuku fukuyu ku mabanja omwe anataya abale awo pofika lachisanu tsabata ino.

Mtsogoleriyu walamulanso komitiyi kuti ithandauzire lipotili mzilankhulo zonse za mdziko muno.

Zipani za AFORD ndi DPP  zidachita zokambirana zawo pamene zipanizi zagwirizana zopanga mgwirizano pa zisankho za 2025.M...
19/12/2024

Zipani za AFORD ndi DPP zidachita zokambirana zawo pamene zipanizi zagwirizana zopanga mgwirizano pa zisankho za 2025.

Mkumanowu udachitikira ku Page house komwe ndi ku nyumba ya mtsogoleri wa chipani cha DPP Professor Aurther Peter Mutharika .

Pakadali pano ndichipani cha AFORD chokha chomwe chabwera poyera kuti chizapanga mgwirizano ndi DPP.

Zipani monga UDF, UTM, PP ndi zipani zina sizidabwere poyera.

Zambiri tikuoatsirani khalani pompo.

19/12/2024

Mtsogoleri wa dziko lino Dr Lazarus Chakwera wati amalawi azigulitsa chimanga matumba awiri mkukagula fertilizer thumba limozi.

Akuti aMalawi asamangokhalira kudandaula za kukwera kwa katundu.

Ichi ndi chigawenga chomwe chimasogolera kukhapa anthu omwe amachita mademo mu mzinda wa Lilongwe Sungani chithunzi
14/11/2024

Ichi ndi chigawenga chomwe chimasogolera kukhapa anthu omwe amachita mademo mu mzinda wa Lilongwe

Sungani chithunzi

23/10/2024

This version of Facebook uses less data and works in all network conditions.

Mkulu yemwe anatchuka ndi program ya music splash pa MBC TV  yemwe dzina lake anali Geoffrey Kapusa pena amaziwikanso ku...
23/04/2024

Mkulu yemwe anatchuka ndi program ya music splash pa MBC TV yemwe dzina lake anali Geoffrey Kapusa pena amaziwikanso kuti Mr splash wamwalira lero atadwala kwa nthawi yaitali.

Address

Area 6
Lilongwe Area 6
24HRS

Telephone

+265999952444

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Malawi online posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Organization

Send a message to Malawi online:

Share