26/01/2023
Muli bwanji amalawi azanga?
Vuto la Kennedy likanalipo chomwe takwanisa ndikumupanga Kennedy kuti abwerereso Ku sukulu.
Tikunena Pano Kennedy akupitiliza maphuzilo Ake pa nkhono primary school.
Tikupemphabe akufuna kwa bwino kuti tizimuthandizabe Kennedy ndi ndalama yoti azipita nayo Ku chipatala kukapopesa madzi omwe akutumpisa mimba take.
Zikomo kwambili kwa omwe mwatengapo gawo pa moyo wa Kennedy.