I love Ngala

I love Ngala I love ngala,do you? if you do, like the page and invite your friends.

kuzaza ka 5litre aka basitu perekani 27pin or 25pin. B13 imeneyi Ngala ya Ku Nkhotakota
12/05/2026

kuzaza ka 5litre aka basitu perekani 27pin or 25pin.

B13 imeneyi Ngala ya Ku Nkhotakota

12/05/2026

welcome to B13 Market.

pamene madzi akuphwera Ku B13 Ngala Railways
12/05/2026

pamene madzi akuphwera Ku B13 Ngala Railways

madzi Aja asunthako sopano. B13 lero
12/05/2026

madzi Aja asunthako sopano.

B13 lero

Utsiku watha MMA 11 pomwe magetsi amazima pa likuchi zapezeka kuti anali akuba omwe aba zipangizo za pa transformer ya p...
11/05/2026

Utsiku watha MMA 11 pomwe magetsi amazima pa likuchi zapezeka kuti anali akuba omwe aba zipangizo za pa transformer ya pa likuchi NDI zina zambiri.

ma report afika kale Ku police NDI Ku eskom tikudikira mayankho komanso zimenezi ndizonkubwezeretsa chitukuko mbuyo. aka sikoyamba .

WA lero. kabigiri NDI k27000 ena 25000.Ngala Ngala!!!!
11/05/2026

WA lero. kabigiri NDI k27000 ena 25000.

Ngala Ngala!!!!

kungala kwacha bwino Kaya uko
11/05/2026

kungala kwacha bwino Kaya uko

08/05/2026

Lero kunali maliro amwana WA miliam WA Kwa mnjiri amene anakwatira Ku chidebwe .

Maliro taika lero pa likuchi .

Pepani akubanja💔😭

Anamangidwa chifukwa choba chimanga ndipo pambuyo pake anatulutsidwa pa bail.Patangopita masiku ochepa, anabanso nkhuku ...
08/05/2026

Anamangidwa chifukwa choba chimanga ndipo pambuyo pake anatulutsidwa pa bail.

Patangopita masiku ochepa, anabanso nkhuku ndipo anthu ammudzi anamumenya kwambiri. Apolisi anamumanganso ndipo anam’tumiza kuchipatala kuti akalandire chithandizo.

Koma ali kuchipatala komweko, anabanso foni ya nurse 🙄

Tsopano nkhani yake ndi yakuti apolisi akukana kumubweza ku station chifukwa tsiku lina limene ankakhala m’maselo, foni yaing’ono ya OC inasowa ndipo pambuyo pake iye anavomera kuti ndi iyeyo amene anabera.

03/05/2026

ndi angati omwe lero anapita ku church

hon Dorophy chikonje posted this....
02/05/2026

hon Dorophy chikonje posted this....

Address

M5 Lake Shore Road
Dwangwa

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when I love Ngala posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share