HAND for the NEEDY youth empowerment club

Directions

HAND for the NEEDY youth empowerment club bringing a brighter future to Malawian youths

21/10/2024

Sizikuonaso kuti udapanga za accounts. Maluzi akuswa aliyese chimodzimodzi ๐Ÿ˜…๐Ÿคฃ

20/10/2024

Ukhale mzibambo wa mimba yayikulu koma osauka. Amakumana chakudya ukuona. Ati awa akadya ku restaurant ๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚ good morning ๐ŸŒž

18/10/2024

Tag mzanu mmodzi amene always amakhala mmaluzi

Good morning ๐ŸŒ…

17/10/2024

Ma likes sakusunthatu guys
Tikupangadi invite azathu koma?

16/10/2024

Tomorrow get ready for some few businesses omwe safunika mpamba just have bundle enaso just have hands basi

We are building a better Malawi together

"Dear Mai Mbambande,We are deeply saddened to hear about the passing of Gogo Sofeleti Chitenje. Our thoughts and prayers...
16/10/2024

"Dear Mai Mbambande,

We are deeply saddened to hear about the passing of Gogo Sofeleti Chitenje. Our thoughts and prayers are with you during this difficult time.

May the loving memories of Gogo Sofeleti bring you comfort and strength. May her legacy of love, wisdom, and kindness continue to inspire and guide your family.

May God Almighty grant you peace, solace, and fortitude to bear this irreparable loss.

Rest in eternal peace, Gogo Sofeleti Chitenje.

Condolences,

16/10/2024

How much money have you made since morning?

 Guys ,Pali anthu awa asakunamizeni kuti akupeleka ndalama ayi mubesa ndalama zanu.pls dont dare kutumiza ndalama kwa mu...
16/10/2024


Guys ,Pali anthu awa asakunamizeni kuti akupeleka ndalama ayi mubesa ndalama zanu.pls dont dare kutumiza ndalama kwa munthu pamene akuti ukatumiza uwina yochukuka zimenezo ndiboza ,and ngat ena ake muli ndimalingaliro otumiza ndalama 300 thousand kuti muwine 10 million mwanyanao ndipo muchimina malodza anu ameneo ๐Ÿ™„๐Ÿ™„mukuona ngat angangopeleka 10 million ?akunamizani and pali timafana tina tayika ma imfo akuti i have received just now mapazi anu nonse amene mukulenga izi zauchitsiru .osayelekeza kutumiza ndalama kwa agalu awa akubelani ndalama Usaid ndondoneko yake yolandilira ndalama siiyi ayi awa ndi aja amati mwawina malata tumizani 100 pin muzatenge kumaselema awa akubelani ndalama yanu mbuzi za wathu izi.
Pls dont dare kutumiza ndalama kwa munthu cholinga muwinepo yochuluka ayi mubesa ndalama zanuโค๏ธโœŒ๏ธ
ZaZaintos Bazuka

Address

Wilson Bickiel Dedza
Dedza

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when HAND for the NEEDY youth empowerment club posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share