26/04/2026
Tikuwaonawa ndi mai Magret Njaidi ndi ana awo awiri a kwa Musheka 2 ground village Henry STA Mwembele ku Zomba.
Amayiwa nyumba yao inaphya atapita kuchipatala Kwa Chilombo. Ngozi yi inaononga matumba 5 a Chimanga kuphatikizapo zovala.
Tilunena pano anawa alibe ngakhale ma uniform chifukwa onse aphyela mu nyumba momwemo.
Nyumbayi amene anaotcha ndi mwana wa achibale awo, mwanayi ndiwodwala mutu wake sumayenda bwino ndiye anapezelapo mwayi pamene amayiwa anapita ku chipatala.
Imran Bedi Foundation ikupepha kwa akufuna kwabwino kuti tiwathandize anawa ndi ma uniform komanso makope.
Thandizo lanu chikhala chinthu chopambana kwambiri.
Amene mwanva kulankhulika nkati tilankhuleni.
Omwe tili sereous tilankhulane pa 0994127708 WhatsApp