LUSO LANGA Community Foundation

LUSO LANGA Community Foundation A Community-Based Organization dedicated to transforming lives in Chipoka, Salima District, Malawi.

Established in 2017, legally registered in 2023, our mission: promote community development through local giving, ending child marriages, promote education

04/06/2026

Kholo kusambira m'manja mwana. Kusiya sukulu kusankha banja. Atsikana, ukwati umaoneka okongola, koma mukulowamo musanakhwime thupi ndi nzeru, sankhani sukulu.

Luso Langa Community Foundation ndife wokondwa kuti tinapereka maganizo  athu pokhazikitsa buku lomwe likukamba  zokhudz...
03/06/2026

Luso Langa Community Foundation ndife wokondwa kuti tinapereka maganizo athu pokhazikitsa buku lomwe likukamba zokhudzana ndi Sustainable Development Goals (SDGs) bukuli lakhazikitsidwa posachedwa ndi Southern African Trust.

Bukuli ndilimene likhale likuwunikira momwe zinthu zikuyendera mwachitsanzo ngati masomphenya a SDGs akukwaniritsidwa kuchokera m'. m'madera kufikira dziko lonse.

Ife a Luso Langa ndife onyadira komanso okondwa kuti tathandizira kuyika nawo maganizo pa bukhu limeneri.

Tikukhulupirira kuti bukuli lithandiza kugwirizanitsa mapulogalamu a Luso Langa ndi ma SDGs.

Gulu  la Luso Langa Community Foundation, pansi pa pulojekiti yoyendetsera ntchito zonse ya VSO, sabata yatha yaphunzits...
03/06/2026

Gulu la Luso Langa Community Foundation, pansi pa pulojekiti yoyendetsera ntchito zonse ya VSO, sabata yatha yaphunzitsa njira yotchedwa Pair-Wise Ranking ma youth club awiri and akwa T/A Makanjira ku m'boma la Salima. Awa ndi ma youth club omwe Luso Langa ikuwasula kuti akule kuchoka pa youth club kufika youth organisation.

Pair-Wise Ranking ndi njira yothandiza anthu kutengapo mbali yomwe imaonholera anthu ammudzi kuzindikira, kukambirana, ndikupeza mavuto omwe akukhudza madera awo.

Ntchitoyi ikulimbikitsa kutengapo mbali ndi kupanga zisankho pamodzi, kuwonetsetsa kuti maganizo anthu m'midzi akulemekezedwa.

Moses Kazembe wa Luso Langa ndi Mable Chiphaka ndiwo aphunzitsa I (mentor) achinyamatawa luso lotsogolera zokambirana ngati izi mmadera mwawo.

Luso Langa Community Foundation, under VSO's inclusive governance project, last week trained two youths clubs we are men...
03/06/2026

Luso Langa Community Foundation, under VSO's inclusive governance project, last week trained two youths clubs we are mentoring to become youth organisations in Pair-Wise Ranking at T/A Makanjira in Salima. This is a participatory approach that helps community members identify, discuss, and prioritize the challenges affecting their areas.

The exercise encourages active participation and collective decision-making, ensuring that local voices are heard and respected.

Luso Langa's Moses Kazembe and Mable Chiphaka equipped the youths with skills to facilitate similar discussions within their communities.

Luso Langa Community Foundation is pleased to to have contributed our ideas and experiences towards the development of t...
03/06/2026

Luso Langa Community Foundation is pleased to to have contributed our ideas and experiences towards the development of this Sustainable Development Goals (SDGs) Tracking Toolkit recently launched by Southern African Trust.

The manual is expected to serve as an important guide for tracking progress, strengthening accountability, and supporting stakeholders in measuring how far the SDGs are being achieved at grassroot and national levels.

This is historical, we are proud and excited to have contributed

We believe that this manual will help in aligning Luso Langa programs with SDGs.

Luso Langa Community Foundation recently facilitated a Validation Workshop for Social Norms on Ending Child Marriages in...
26/05/2026

Luso Langa Community Foundation recently facilitated a Validation Workshop for Social Norms on Ending Child Marriages in Chipoka, T/A Ndindi, Salima District. The workshop aimed at engaging the Social Norms Task Force to validate the consolidated views from various community structures on what should be incorporated in the norms.

This follows completion of community consultation meetings during which Luso Langa gathered views and opinions from 210 community members representing different groups.

These included nine child and youth groups, traditional leaders, religious leaders, government officials, and other stakeholders.

Validation ensures community ownership and objectivity in the whole process of developing the norms.

As a Community Foundation, we believe in young people as the foundation of our community. We are committed to employer y...
25/05/2026

As a Community Foundation, we believe in young people as the foundation of our community. We are committed to employer young people, help them to unleash their full potential.

23/05/2026

Luso Langa Youth Club, a youth development platform under Luso Langa has officially received a Registration Certificate from the office of the District Youth Office (Salima), confirming that the club is now officially recognized at district level.

This development allows the youth club to officially carry out its activities within the Chipoka area while working closely with and reporting to the District Youth Office.

The certificate handover ceremony took place at Mchoka Resource Center, T/A Ndindi in Salima

Members of Luso Langa Youth Club have welcomed the approval, saying it will help strengthen youth development programs, community participation, and empowerment initiatives in Chipoka.

National Initiative for Civic Education (NICE) ochokera ku  ofesi ya Salima, posachedwapa anaphunzitsa achinyamata 15 oc...
22/05/2026

National Initiative for Civic Education (NICE) ochokera ku ofesi ya Salima, posachedwapa anaphunzitsa achinyamata 15 ochokera ku gulu la Luso Langa Community Foundation pankhani ya ndondomeko ya Malawi Vision 2063.

Pamsonkhanowo, womwe unachitikira pasukulu ya pulaimale ya Chipoka 1, akuluakulu a bungwe la NICE anaunikira achinyamatawo njira zosinthira maganizo a anthu ammudzi, kuti dziko la Malawi likhale lotukuka.

Bungwe la NICE lalimbikitsa gulu la Luso Langa kuti adziwitse anthu a m’dera la Chipoka kuti amvetsetse kufunikira kokhala ndi maganizo abwino ndi kuika maganizo awo pa kukwaniritsa zolinga za chitukuko chokhazikika.

Polankhula pamsonkhanowu, akuluakulu a NICE anati anachita chidwi ndi momwe Luso Langa ikugwirira ntchito ku Chipoka, ndipo awonetsa chidwi kugwira ntchito limodzi ndi luso Langa.

Kodi MwavaAchinyamata okwana anayi a gulu la Luso Langa Community Foundation alinawo mgulu  la maphunziro a masiku atatu...
22/05/2026

Kodi Mwava

Achinyamata okwana anayi a gulu la Luso Langa Community Foundation alinawo mgulu la maphunziro a masiku atatu la Inclusive Governance and Youth Mentorship okonzedwa ndi Volunteers Services Overseas (VSO) ku Rivermark Lodge ku Salima.

Zina mwazomwe akuphunzira ndi njira zoyika patsogolo chitukuko kumagulu a anthu, komanso luso lowonetsetsa kuti anthu omwe alibe chidwi atenga nawo mbali mofanana.

Kumapeto kwa maphunzirowa, omwe atenga nawo mbali apatsidwa makalabu a achinyamata ku Salima kuti aziwaphunzitsa ma kalabuwo kuti afike pa ma Youth organization.

Mable Chiphaka, Lukila Chiwaya, Moses Kazemba, and Bezita Chibungwe ndamene anayimirira Luso Langa Community Foundation.

Address

Luso Langa Community Foundation, P. O Box 74
Chipoka

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when LUSO LANGA Community Foundation posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Organization

Send a message to LUSO LANGA Community Foundation:

Share