29/07/2026
Masiku anotu zodalira amalume kapena aunt aku tawuni kuti atigaire ndalama zinatha. Phuzirani ntchto za manja zomwe wina sangakulandeni mutaphuzira. Ife a vision for Development Youth training college tikukuitananiso ku maphuziro aza luso omwe tayambaso kupereka tsopano. Monga kusoka zovala, za magetsi, kaphikidwe ka makono ndi zina zambiri tabwerani muzaphuzire pa mtengo ovelera fizi yathu ndiyosaboola nthumba K220,000 yokha basi inu muphuzira nawo kwa miyezi isanu ndi umodzi (9 months)
Mukafuna kudziwa zambiri tchayani lamya pa +265 886 868 686
Empowering youth through vocational skills