07/03/2026
🌿Ngati mukufuna ndalama yachangu changu Wina angokudabwitsani
🌿Lembani chizindikiro cha infinity Ichi👉 ♾️ pa dzanja lanu lakumanzere kapena pankono.
Kenako mukalemba Wazanipo cinnamon pang’ono pamwambapo cinnamon powder.
🌿 Ganizirani za ndalama zomwe mukufuna.
🌿 Yerekezani Kaya mukufuna k10000 ngati muli kale ndi ndalama zimenezo yankhulilani.
🌿mosayembekezereka kapena mwadziidzidzi, mulandira ndalama zomwe mukufuna.
🌿 Mwayi watsopano wopangira ndalama ungatseguke, kapena
🌿 munthu wina angakudabwitseni ndi ndalama zomwe mukufuna kapena winawake alindindalama yanu anakubwerekani kalekale ,Kaya wachibale alikujon muzadabwa akukutumizilani njila zambilimbili mulungu apanga njila ndithu mpaka munapatsidwa.
🌿 Khulupirirani mphamvu ya Chilengedwe.
🌿Bambo a Yewo from ekwenden