23/11/2025
Mudzi omwe umasamalira achikulire umayenda nkuunika kwa Mulungu.
Achikulire ndi mdalitso.
M’busa Pilira Chibwana wa mpingo wa Mulunguzi community akutikumbutsa kuti kusamalira achikulire si ntchito yosiyirana koma ndi udindo omwe Mulungu anaupereka kwa ife tonse.