MISI

Website

MISI Supporting Madrassah students and Imams 🤲 | Promoting Qur’an education 📖 | Building a stronger Ummah 🕌 | Follow, share & support MISI

Zolinga za misi ndi tsogolo la ummah,Ana athu alimbikitsidwe PA maphunziro awo adeen komanso ma shekh akhale ma role mod...
10/08/2026

Zolinga za misi ndi tsogolo la ummah,Ana athu alimbikitsidwe PA maphunziro awo adeen komanso ma shekh akhale ma role model kwa Ana

Support misi. Muslimah In Islam muslim

28/06/2026

Maa shaa Allah imvani izi mwina simunali kudziwa by shekh shuayb lamusi patero

Tikhale ndi jumuah yopambana osaiwala kuwelenga surat Al-kahf,komanso kusamba lero ndi sunnah baraaka llah fikum.       ...
26/06/2026

Tikhale ndi jumuah yopambana osaiwala kuwelenga surat Al-kahf,komanso kusamba lero ndi sunnah baraaka llah fikum.

🧕 KUPEMPHA THANDIZO LA MA HIJABU 🧕MISI (Madrassah and Imam Support Initiative) ikupempha anthu onse achifundo kuti athan...
25/06/2026

🧕 KUPEMPHA THANDIZO LA MA HIJABU 🧕

MISI (Madrassah and Imam Support Initiative) ikupempha anthu onse achifundo kuti athandize pa ntchito yogawira ma hijabu kwa ana ndi azimayi osowa.

Thandizo laling'ono, phindu lalikulu. Hijabu imodzi yomwe mungapereke ingakhale chifukwa chopezera munthu madalitso ndi chisomo cha Allah.

📞 Director wa MISI:
• 0994475572
• 0894506677

Allah alandire sadaka yanu ndi kukudalitsani kwambiri. Ameen.

🌙 SUNNAH FASTING OF MUHARRAM (9th & 10th) 🌙Musaphonye mwayi wa madalitso m'mwezi wolemekezeka wa Muharram.Mtumiki ﷺ anat...
23/06/2026

🌙 SUNNAH FASTING OF MUHARRAM (9th & 10th) 🌙

Musaphonye mwayi wa madalitso m'mwezi wolemekezeka wa Muharram.

Mtumiki ﷺ anati:

"Kusala kwa tsiku la Ashura kumafafaniza machimo a chaka chapitacho." (Sahih Muslim)

Tikulimbikitsa Asilamu onse kusala pa 9th ndi 10th Muharram potsatira Sunnah ya Mtumiki ﷺ.

✅ Funsani chikhululukiro kwa Allah
✅ Limbikitsani Taqwa yanu
✅ Chulukitsani Du'a ndi zikumbutso za Allah
✅ Chulukitsani ntchito zabwino

Allah atipange kukhala m'gulu la osala ndi kulandira ntchito zathu zabwino.

📖 MISI – Madrassah and Imam Support Initiative
Empowering Madrassah Children • Supporting Imams • Strengthening the Ummah

📲 Follow MISI on:
Facebook | TikTok | YouTube | Instagram | X (Twitter) | WhatsApp

📞 Contact: 0994475572

Why Choose MISI?1. We Focus on Islamic EducationMISI is dedicated to strengthening Madrassah education by helping childr...
23/06/2026

Why Choose MISI?

1. We Focus on Islamic Education
MISI is dedicated to strengthening Madrassah education by helping children learn the Qur’an and Islamic knowledge.

2. We Support Imams and Teachers
Imams and Madrassah teachers are the backbone of our communities. MISI works to support and encourage them in their noble mission.

3. We Care for Underprivileged Children
Many Madrassah students come from vulnerable backgrounds. MISI seeks to empower them through educational and welfare support.

4. We Promote Community Development
Through education, awareness programs, and charitable initiatives, MISI contributes to building stronger Muslim communities.

5. We Encourage Transparency and Accountability
We strive to ensure that donations and support are used responsibly for the benefit of Madrassahs, Imams, and students.

6. We Work with the Community
MISI believes that lasting change comes through cooperation between Imams, teachers, donors, parents, and the wider Muslim community.

7. We Are Driven by Islamic Values
Our work is guided by sincerity (Ikhlas), trustworthiness (Amanah), compassion (Rahmah), and service to the Ummah.

8. Every Contribution Makes a Difference
Whether through donations, volunteering, sharing our message, or making du‘a, every supporter helps us advance the cause of Islamic education.

Our Promise
By supporting MISI, you are investing in Qur’anic education, empowering Madrassah children, supporting Imams, and helping build a stronger future for the Ummah.

MISI – Madrassah and Imam Support Initiative "Empowering Madrassah Children, Supporting Imams, Strengthening the Ummah." 🤝📖🕌

22/06/2026

Zimvereni nokha nde chitsankho mupanga mukamveramo by shekh shuayb lamusi patero.

Zolinga za MISI welengani mofatsa ndithu muzimvetsetse.
21/06/2026

Zolinga za MISI welengani mofatsa ndithu muzimvetsetse.

Address

Malosa Zomba
Zomba
304105

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when MISI posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share