09/09/2025
MNSONKHANO WOYIMAYIMA
Mmawa pa 10th September 2025, lomwe ndi lachitatu. A President Dr Lazarus Chakwera akhale ndi mnsonkhano woyendera anthu ku Nsanje North ( whistle Stop Tour)
A President Chakwera azakhale akuima pa Chinyanje Trading Centre kenako azakafika pa Fatima Boys, tiyeni tonse tizakhamukire mmadera tatchulawa ndikuzamvera mfundo za Chitukuko.
Achinyamata, azimayi, azibambo nthawi yakwana taono imene Tate wafuko akufuna kuzacheza nanu. Ndipotu game iyiyi, ndi Wadya Mtoliro.
Vote for Enock Chizuzu MP, vote for Dr Lazarus McCarthy Chakwera- President of the Republic of Malawi