SMALL WORLD

SMALL WORLD A home away from home.. LEARNER'S today, LEADERS tomorrow.

04/12/2023

Omwe timayakhula ziyankhulidwe izi

Chitumbuka
Chilomwe
Chiyawo
Chilambia
Chiswahiri
Chitonga
Chinkhonde
And other languages please inbox... Or mundiuzeko kuti mawu awa muchiyankhulo chanu mati bwanji

"" muli mbwanji
Takulandilani
Tukufunilani Christmas yopambana"""

My children have an activity on malawi languages

Send a msg or vn through 0993349599 on WhatsApp or fb inbox

Uyu ndi emelesia phiri wazaka 17 zakubadwa. Atamwalira makolo ake onse ndi mavuto amakumana nawo anaganiza zongosiya suk...
12/11/2023

Uyu ndi emelesia phiri wazaka 17 zakubadwa. Atamwalira makolo ake onse ndi mavuto amakumana nawo anaganiza zongosiya sukulu ndiku kwatiwa. Emelesia adakwatiwa Ali ndi zaka 15 Ndipo anathawako ku banja Ali ndi zaka 16 kamba kamavuto amakumana nawo. Pano Ali ndi zaka 17 Ndipo a kuganiza zobweleranso kusukulu yomwe adasiyira STD 8.
Emelesia akuti atha kuyambilando STD 7 kuti azachite bwino STD 8 ngati kuthekela ndi upangiri ungapezeke kuti abwelelenso ku sukulu.
Anthu akufuna kwabwino ndi omwe amulumikizitsa mtsikana yu ndiine Ndipo ndacheza naye and chidwi chobwelelanso ku school chilimo..

Kwaomwe a ngakwanitse kumunthandiza mtsikana yu chonde tiyeni timuthandize.. Kaya ndi chikwama, makope, uniform and school fund/feesπŸ™πŸ™πŸ™πŸ™πŸ™
Call 0993349599 /0882015215 FOR MORE INFORMATION

31/10/2023

Am so sad😭😭😭 one of my kid came today early morning around to 5 am and akundiuza kuti her dad amuuza asiye school azikalima ku lusangazi 😭😭 she's just 15 years in Std 5 samkachita bwino because kale samapita ku school amangokhalira kumunda nde za school munalibe but since I took her when she was in Std 4 pano improvement ilipo yambiri zedi basi bambo ake aziti asiye school lero.

I dont know what to do abale.

We have received cloths from some well wishers..... On behalf of my children and Small world child Edu-care centers I wo...
28/10/2023

We have received cloths from some well wishers..... On behalf of my children and Small world child Edu-care centers I would like to thank you for your help and kindness upon these children. May God bless you so so muchπŸ™.

Building a home away from home.... Our kids are blessed together with the community
28/10/2023

Building a home away from home.... Our kids are blessed together with the community

Today we received 6 unit of note books and 1 box of pens from a well wisher..... I shared the books to some of my childr...
23/10/2023

Today we received 6 unit of note books and 1 box of pens from a well wisher..... I shared the books to some of my children (9) Ngakhale ena omwe sanalandile nawo anayamba kulira koma nayesesa kuwauza kuti next time azalandira ndi wowo....

15/10/2023
Before and after receiving the cloths..... Thanks to every hand that donated God bless you
05/10/2023

Before and after receiving the cloths..... Thanks to every hand that donated God bless you

20/09/2023

We are in week 2 and the STD 1s have ordy started reading...... Am a proud teacher πŸ’ƒπŸ’ƒπŸ’ƒ

14/09/2023
As we are in first week..... Look at how precious the kids look... They missed school so much
14/09/2023

As we are in first week..... Look at how precious the kids look... They missed school so much

Address

Mzuzu

Telephone

+265993349599

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when SMALL WORLD posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share