SHAMA orphan & charitable group

SHAMA orphan & charitable group Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from SHAMA orphan & charitable group, Nonprofit Organization, Mulanje.

19/08/2023

Tikumbusane kuti Tisawasale amasiye ndi Okalamba komaso Olumala

Zina mwazomwe Tikupanga
15/08/2023

Zina mwazomwe Tikupanga

Came and join me to help people
08/04/2023

Came and join me to help people

26/03/2023

Chimphuzitso, Kod mukuziwa kuti kuimisa zala ziwili zitathauza kuti tilipo awili ine ndi satana. Kuimisa Chala chimodzi kuthauza kuti alipo modzi satana yekha samalani ndimachelelo asatana Aifeso 6 vs 11-12

26/03/2023

Akufuna Kwabwino, came and join Shama Charity Organization malawi, kalikonse komwe muli Nako, azanthu akusowa ngakhale supuni join me to help people 0888474122

Mogokumbusana shama Charity Organization, ikupiliza kugwila nchito zake makaso nyingo yovuta ino. Akufuna Kwabwino Tabwe...
26/03/2023

Mogokumbusana shama Charity Organization, ikupiliza kugwila nchito zake makaso nyingo yovuta ino. Akufuna Kwabwino Tabwelani Tigwilane manja ndikuthandiza anthu Omwe Ali mumvuto azawoneni.

Mwini wake washama ndi ameneyu, tiyeni tithandizane potukula ndikuthandiza dziko lanthu.
23/03/2023

Mwini wake washama ndi ameneyu, tiyeni tithandizane potukula ndikuthandiza dziko lanthu.

Osaiwala kuti ife Eni ake Ashama Tikupitiliza kuthandiza Amasiye Olumala ndi Okalamba. Came and join 0888474122.
23/03/2023

Osaiwala kuti ife Eni ake Ashama Tikupitiliza kuthandiza Amasiye Olumala ndi Okalamba. Came and join 0888474122.

08/03/2023

Unthenga wabwino kwanonse akufuna kwabwino.

Osalema pakuchita  zabwino. Tiyeni tigwilane manja call 0888474122
08/03/2023

Osalema pakuchita zabwino. Tiyeni tigwilane manja call 0888474122

Ndithokoze ambuye. Chifukwa chanonse Omwe mwathandiza  Umoyo wabanja ili ambuye akusamalileni ndikukutetezani. Yohane 15...
08/03/2023

Ndithokoze ambuye. Chifukwa chanonse Omwe mwathandiza Umoyo wabanja ili ambuye akusamalileni ndikukutetezani. Yohane 15 vs 7. Ikulondoleni amen.

I like anthu ngati awa tisawasale
07/03/2023

I like anthu ngati awa tisawasale

Address

Mulanje

Telephone

+265888474122

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when SHAMA orphan & charitable group posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share