CHRR Malawi

CHRR Malawi The Centre for Human Rights and Rehabilitation (CHRR), is one of the leading human rights and good governance local non-governmental organisations in Malawi

13/07/2026

Sabata iliyonse yatsopano, imatikumbutsa kuti tili ndi mwayi woyimirira ufulu wa anthu, kulimbikitsa kufanana, komanso kukweza mawu a anthu m'madera osiyanasiyana m'dziko lino..

Ku CHRR, tikupitirizabe kudzipereka polimbikitsa chilungamo, kuteteza ufulu wa munthu aliyense, komanso kugwira ntchito limodzi ndi nzika, mabungwe othandizana nawo, ndi mabungwe aboma kuti timange dziko limene ufulu wa munthu aliyense ndiolemekezedwa ndi kutetezedwa.

Pamene tikuyamba sabata ino, tiyeni tonse tigwire nawo ntchito yolimbikitsa ulemu wa munthu, kufanana, ndi ufulu kwa aliyense.

Tikagwirizana, titha kumanga Malawi amene ufulu wa munthu aliyense ndiolemekezedwa.

Happy Independence Day Malawi!
06/07/2026

Happy Independence Day Malawi!

PRESS RELEASE.
02/07/2026

PRESS RELEASE.

CHRR pamodzi ndi mabungwe ena a  Civil Society Organisations(Cso's  linatenga nawo mbali pamsonkhano woyambilira (onboar...
30/06/2026

CHRR pamodzi ndi mabungwe ena a Civil Society Organisations(Cso's linatenga nawo mbali pamsonkhano woyambilira (onboarding meeting) womwe unakonzedwa ndi HIVOS Malawi pansi pa ntchito ya Connect, Defend, Act! kuyambira pa 24 mpaka pa 25 june 2026.

Msonkhanowu unali chiyambi cha mgwirizano wolimbikitsa ubale pakati pa mabungwe komanso kupititsa patsogolo ntchito zoteteza ndi kulimbikitsa malo omwe anthu angathe kutenga nawo mbali pa nkhani za dziko mwaufulu.

CHRR ikuthokoza kwambiri mwayi wogwira ntchito limodzi ndi HIVOS Malawi komanso mabungwe anzathu pothandiza kulimbikitsa ufulu wa anthu, kutenga nawo mbali kwa nzika pa nkhani za dziko, ndi mfundo za demokalase kuti zipitirire kukula kuno ku Malawi.

We continue to witness the positive impact of the Strengthening Support Groups of Women Living with HIV and AIDS Project...
17/06/2026

We continue to witness the positive impact of the Strengthening Support Groups of Women Living with HIV and AIDS Project, funded by the Stephen Lewis Foundation.

Recently, we visited Mitundu, TA Kalolo, where we met members of the Mapuyu and Nyanja Support Groups. The groups received financial support in 2012 and 2021, and since then, the women have participated in various trainings and awareness meetings aimed at strengthening their business and financial management skills.

Through this support, many women have been able to start and expand small businesses, improve their household incomes, and better support their families. The groups have also provided a strong network of encouragement, helping members build confidence, share experiences, and face challenges together.

These photos showcase the incredible women of Mapuyu and Nyanja Support Groups.

As we look back on the 2025 General Elections, CHRR is proud to have contributed to promoting peaceful, inclusive, and i...
09/06/2026

As we look back on the 2025 General Elections, CHRR is proud to have contributed to promoting peaceful, inclusive, and informed electoral participation through civic education trainings and community outreach activities conducted across Malawi under the UNDP-supported project on Inclusive and Peaceful Electoral Participation.

Ahead of the elections, CHRR engaged hundreds of participants—including persons with disabilities, women, youth, traditional leaders, and community members—on human rights, electoral laws, peaceful coexistence, and the prevention of electoral violence.

At a time when misinformation, political intolerance, and tensions had the potential to divide communities, these engagements provided safe spaces for dialogue, learning, and collective action. Participants gained knowledge about their electoral rights and responsibilities, how to report violence, and the importance of rejecting hate speech and political intimidation.

The impact was evident in the peaceful participation witnessed in many communities during the electoral period. Traditional leaders strengthened local peacebuilding efforts, vulnerable groups became more confident in engaging in electoral processes, and communities demonstrated greater appreciation for tolerance, inclusion, and democratic accountability.

Importantly, persons with disabilities were given platforms to raise concerns about accessibility, representation, and voter autonomy. These conversations encouraged communities and stakeholders to promote equal participation and safeguard the rights of every voter.

The accompanying photos capture some of the powerful moments from CHRR’s outreach and training activities in Blantyre and Mzuzu.

CHRR remains committed to advancing human rights, peaceful coexistence, and inclusive democratic participation for all Malawians.

Malawi


06/06/2026

The Centre for Human Rights and Rehabilitation (CHRR) recently conducted a community awareness campaign in Goup Village Head Mtanda, Traditional Authority Khombedza in Salima District to promote the inclusion and support of women living with HIV in community activities.
The campaign focused on raising awareness about the challenges faced by women living with HIV, including stigma and discrimination, denial of participation in community activities, and property grabbing following the death of a spouse. Community members were also encouraged to practice safe s*x and undergo regular HIV testing, particularly in lakeshore communities where high-risk s*xual behaviors are prevalent.
Speaking during the awareness session, Group Village Head Mtanda observed that many men in his area experience gender-based violence but often fail to seek help because most support services and interventions are primarily targeted at women.
The awareness campaign was implemented under the Strengthening Support Groups of Women Living with HIV and AIDS Project, which is funded by the Stephen Lewis Foundation.

Ngati gawo limodzi la ntchito ya Strengthening Support Groups of Women Living with HIV and AIDS, yomwe ikuthandizidwa nd...
03/06/2026

Ngati gawo limodzi la ntchito ya Strengthening Support Groups of Women Living with HIV and AIDS, yomwe ikuthandizidwa ndi Stephen Lewis Foundation, bungwe la Centre for Human Rights and Rehabilitation (CHRR) linachita ulendo wowunika momwe zinthu zikuyendera kwa amayi omwe ali ndi HIV/AIDS omwe adapindula ndi thandizo loyambitsa mabizinesi awo mu zaka za 2022 ndi 2024 m’dera la Group Village Head Kasonda, T/A Khombedza m’boma la Salima.
Ulendowu unayang’ana magulu awiri othandizana m’dera la T/A Khombedza, Salima, omwe ndi Tikondane Group (mamembala 43) ndi Chiembekezo Group (mamembala 35).
Amayiwa ayika ndalama zawo m’ntchito zosiyanasiyana zopangira ndalama monga kuweta ziweto, ulimi wa njuchi, komanso mabungwe osungirana ndi kubwereketsana ndalama (Bank Mkhonde), zomwe zawathandiza kusamalira mabanja awo ndi kukwaniritsa zosowa za tsiku ndi tsiku.
Maguluwa ananenanso kuti akufunika thandizo lina komanso mwayi wophunzitsidwa luso lina, makamaka la ndi kusoka zovala (utelala), zomwe zingawathandize kuwonjezera njira zopezera ndalama komanso kulimbikitsa kudziyimira pawokha pa chuma.
Maguluwa anakhazikitsidwa mu chaka cha 2019 ndipo anayamba kuthandizidwa ndi CHRR mu zaka za 2022 ndi 2024.

26/05/2026

Mongokumbutsana….
Ufulu wa munthu si mwayi wa kwa anthu ochepa chabe, koma ndi wa aliyense.
Tiyeni tipitirize kulimbikitsa chilungamo, kufanana, ndi ulemu wa munthu aliyense. Tikamateteza ufulu wa anthu, tikuteteza umunthu wathu tonse.
Pamodzi tingamange dziko limene ufulu wa anthu umatetezedwa ndipo palibe amene amasiyidwa m’mbuyo.

Address

24 Mango Street, Area 47, Sector 3
Lilongwe

Opening Hours

Monday 08:00 - 16:30
Tuesday 08:00 - 16:30
Wednesday 08:00 - 16:30
Thursday 08:00 - 16:30
Friday 08:00 - 13:00

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when CHRR Malawi posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share