02/05/2026
Kodi mukudziwa kuti m***a kuphunzira ntchito zama Luso amanja kwa ULERE? π
Ife a International Youth Fellowship (IYF) tili okondwa kukudziwitsani kuti takubweretsani IYF Weekend Academy Session 2 β pulogalamu yapadera yopatsa achinyamata luso lomwe lingakuthandizeni kukhala odzidalira komanso kuyambitsa bizinesi yanu payokha! πΌπ₯
π Maphunziro omwe alipo:
β’ Computer Basic
β’ Camera Operation
β’ Plumbing
β’ English
β’ Business Management
β’ Carpentry & Interior Designing
β’ Cosmetology (Beauty & Hairdressing)
β’ Electrical & Solar Systems Installation
β¨ Ubwino wake:
β’ Ma phunziro onse ndi a ULERE, Mumangofunsidwa Kulipila K10, 000 yolembetsera Yokha basi
β’ Mupatsidwa Certificate mukamaliza
β’ Muphunzira luso logwira ntchito zenizeni
π Malo: Area 25A Achievers PVT School (Kumbuyo kwa Nyumba Ya Skefa Chimoto )
π Nthawi: Loweruka & Lamlungu Lililonse Kuyambira 9:00 Koloko Mamawa Mpaka 12 Koloko Masana
π
Kutsegulira Pa: 9th May 2026
β οΈ Malo ndi ochepa β Oyamba Kubwera, Oyamba Kulembetsedwa!
π Lumikizanani nafe Pama nambala awa kuti mulembetse:
0982 572 777 / 0882 251 516
π₯ Osaphonya mwayi uwu! Bwerani mudzasinthe tsogolo lanu kudzera mu luso!