02/04/2026
Amene tilibe MSCE ya bho, ngati mpata ulipo chonde pangan zoti mulembe mayeso next yr. Zilibe kanthu k*t mudzasowa nayo kolowera or so, koma khalan ndi certificate ya bho.
Amene tili kale ku xu ndipo tupanga zoti tilembe, limbikirani. Use that opportunity wisely kupewa zitonzo k*tsogoloku.
Anthu akudandaula kunjaku, failing to excel fukwa MSCE sili bho. Akukanika kupanga upgrade or kuonjezera opportunities fukwa pali chiblock cha under-qualified MSCE.
Umboni wa zomwe tunenazi nd azibambo ndi azimayi omwe amaphunzira sukulu za night. Kumapezeka ena oti ali pa ntchito kale like nurses, primary school teachers, clinical officers, accountants, etc or ena oti amayenda chokhala koma mkudzichepetsa kudzakonza kumbuyo.
2023/24 academic year, we had a student amene anaphonya mwayi wovaya abroad to study nursing fukwa chosowa MSCE ya bho. Well wisher wochokera ku church kwawo "mngerezi" atapezeka k*ti amuphunztse fukwa cha khama lake lokonda za praise and worship.
Mukakonzeka kujudulanso MSCE ife tilipo timuthandzan. M***a kumapanga mobisa mkuzangodzidzimutsa chigulu mutakwapula ka teen ka bho. With just our online classes titha kuchunani ma subject omwe mungasankhe k*t muzawakwapule bho. It's you and your phone, bola data k*ti MSCE muzainyapule.
Tilinso ndi ena omwe ali ku dyubeki, akuphunzira online. Tinawapangira register kwina kwake while abroad moti abwera May kuyamba zokonzekera kenako kubwereranso ku magobo after kulemba mayeso without knowledge of their relativesπ
Zungofunika kulimba mtima basi.
For WhatsApp Classes 0882 43 55 62
fans