05/08/2026
Pa mudzi pano ndikufuna munthu oziwa kumanga zomanga Manga kaya manyumba maka makhola ngati alipo bale wanu ndiuzeni
Komaso ndikufuna munthu yemwe amatha kupanga ndikuweta nkhuku za chizunguzi ndi mikolongwe komanso ziziri ndufuna oziwa zonsezi mene nkhuku imakulisilidwila kuchoka pa anapiye kufika pogulisa koma komaso pa unapiye kufika poikila madzila honest and liable person
Together we can make better malawi