13/11/2025
Alezi omwe mukupeleka Chisamaliro Kwa ana aulumari
✋ L E K A N I !
kutsekera Mnyumba ana omwe ndi aulumari
kutsekera Mnyumba ana omwe ali ulumari ndi mulandu, mukapezeka muzaimbidwa mulandu
Tiyeni tibwere poyera, ulurani nkhanza zomwe ana aulumari akukumana nazo mdera lathu
poimba foni ya ulere ya
1 1 6
(YONECO child Helpline)
kapena ku Police (VSU Office) yomwe muli nayo pafupi
Mwana atetezedwe, Mwana alandire Chisamaliro, Mwana aphunzire, mwana akhale ndi ufulu,
Machinjiri Child Protection Case Conference
UNICEF Malawi
YONECO FM
Youth Net and Counselling (YONECO)
Youth Activists Initiative Organization
Malawi Police Service
Active Youth Association.
World Vision Malawi